UTATU Woyera Parish YOUTH

UTATU Woyera Parish YOUTH Utatu woyera youth movement

23/08/2026
kwangotsala ma hours πŸ₯³πŸŽ‰
20/08/2026

kwangotsala ma hours πŸ₯³πŸŽ‰

Ana okwana 51 ndiomwe alandira sacrament la ukaristia dzulo Ku utatu woyera parish omwe  anatsogolera mwambowu Fr kanyam...
17/08/2026

Ana okwana 51 ndiomwe alandira sacrament la ukaristia dzulo Ku utatu woyera parish omwe anatsogolera mwambowu Fr kanyambo alimbikitsa anawa Kuti akhale akhristu olimba komanso odalirika mu mpingo

For youth .By youth.
14/08/2026

For youth .By youth.

See You at St John's Secondary School!

Tiyen Tiyen πŸ₯³
09/08/2026

Tiyen Tiyen πŸ₯³

Tick Tock!

Mtima Woyera Deanery Youth Catholic Archdiocese of Lilongwe

07/08/2026

Pamene achinyamata aku utatu woyera parish akupitilira nd fundraising yawo mu sabatayi lero anayendera mphakati wa st Andrew's ndi st Agnes

YOUTH POWER πŸ’ͺ!!!

Ngati njira imodzi yofuna kupeza ndlama zoyendetsera gulu la achinyamata pa utatu woyera parish kawale achinyamata apa p...
06/08/2026

Ngati njira imodzi yofuna kupeza ndlama zoyendetsera gulu la achinyamata pa utatu woyera parish kawale achinyamata apa parish yi akuyendera mphakati Kuti azigwira ma ganyu ndpo kangachepe apezeko aike kuthumba lawo.

14/07/2026
14/07/2026

Currently Trending
Lady of Fatima
Parish

Tiyen Ife achinyamata amumpingo wa katolika tikhale achikondi ndi ochita zabwino.πŸ™
14/07/2026

Tiyen Ife achinyamata amumpingo wa katolika tikhale achikondi ndi ochita zabwino.πŸ™

Address

Lilongwe

Telephone

+265888073150

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when UTATU Woyera Parish YOUTH posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share