Holly Trinity For All Tribes Church Ministry

Holly Trinity For All Tribes Church Ministry Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Holly Trinity For All Tribes Church Ministry, Religious organisation, Area 25 A. along the Road from 25A to Nsungwi, Lilongwe.

02/08/2026

Church Service

Thanks to all who supported financially and physically.Not forget those who were engaged in prayer for this.All in all w...
26/07/2026

Thanks to all who supported financially and physically.

Not forget those who were engaged in prayer for this.

All in all we thank God

Tilipano kuchita umboni Kuti ZATHEKA

TOMBSTONE UNVEILING
05/07/2026

TOMBSTONE UNVEILING

21/06/2026

Kutengela pa buku la Yona 1. Kodi ntchito imene mulungu wakutumani ndi chani. Ngati mwayithawa, mavuto sakusiyani mpakana ntchitoyo mutayigwira.

21/06/2026

Jona 1: 1 kupita mmusi

1Yehova anayankhula ndi Yona mwana wa Amitai kuti, 2 “Nyamuka, pita ku mzinda waukulu wa Ninive ndipo ukalalikire motsutsana nawo, chifukwa zoyipa zawo zafika pamaso panga.”
3 Koma Yona anathawa Yehova ndi kulowera ku Tarisisi. Anapita ku Yopa, kumene anapeza sitima yapamadzi yopita ku Tarisisi. Atagula chiphaso, anakwera sitimayo kupita ku Tarisisi kuthawa Yehova.
4 Koma Yehova anatumiza chimphepo champhamvu pa nyanja, ndipo panauka namondwe wamphamvu amene anafuna kuphwanya sitimayo.

21/06/2026
08/06/2026

1 Atesalonika 5: 16-18

16 Kondwerani nthawi zonse. 17 Pempherani kosalekeza. 18 Yamikani mu zonse, pakuti ichi ndi chifuniro cha Mulungu kwa inu mwa Khristu Yesu

NOTE: osayiwala kupemphera pachilichonse. Podzuka, poyamba ntchito, pogona komanso muzina zonse

Address

Area 25 A. Along The Road From 25A To Nsungwi
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Holly Trinity For All Tribes Church Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share