19/11/2021
Amalawi anzanga ngati mukudalira kuphuzira ndi kucenjera mukutaya nthawi ,, tapenyani conde conde,, tsekulani makutu anu kuti munvetsere zimene mulungu akufuna kucita ndi dziko amalawi tadzukani conde conde ine sindinaphuzile ngati inu koma ndimamukonda yesu..tayambani kumukonda yesu muona nyengo za dziko lathu la malawi zisintha,palibe comulaka mulungu..ndipo mulungu salakwitsa ai..tamuyesani mulungu muone,mulungu akudalitseni a MALAWI