28/10/2025
Nkhani zina tikamamva zomwe zikuchitika padziko lapansi, pena mutu nkuima,
Koma dziwani kuti ndizizindikiro kuti tiri mmasiku osiriza.
Mulungu, muzaotche moto
Timvereni chitsoni ife monga ana anu. AMEN