Masintha CCAP YOUTH Ministry

Masintha CCAP YOUTH Ministry Why should any of you consider it in CREDIBLE that GOD raises the dead?.......Acts 26 vs 8

Zochita za SundayYou are all invited โค๏ธ๐Ÿ™
01/05/2025

Zochita za Sunday

You are all invited โค๏ธ๐Ÿ™

30/03/2025

The program will be live from 3:00 pm

Be there ๐Ÿ™๐Ÿ™

Takulandilani kuno ku Masintha mukhale nonse omasuka wayitana ndi yesuMwinatu mumangonva mawu uzuna aja Koma mumafuna mu...
26/03/2025

Takulandilani kuno ku Masintha mukhale nonse omasuka wayitana ndi yesu

Mwinatu mumangonva mawu uzuna aja
Koma mumafuna mutadziwa Zambiri kuchokela kwa iwo

This coming Sunday
Masintha CCAP youth ministry ikubweletselani
Mrs Dzonzi inde Inu a choir mistress a Masintha chitsitsimutso women's choir

Ndipo program yi idzakhala live pa page pano from 2:00 pm

Akadzati ODALA NDI ONSEWO aaaa Inu Inu

See you there ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

Come and worship with us  tomorrow
08/03/2025

Come and worship with us tomorrow

Ndi 10,000.00 yokha inuyo mukhoza kugula nsalu imeneyi Nsalu yokongola zedi yoti mukasoketsa chovala anthu chewu chewu k...
26/02/2025

Ndi 10,000.00 yokha inuyo mukhoza kugula nsalu imeneyi

Nsalu yokongola zedi yoti mukasoketsa chovala anthu chewu chewu kumakusililani

Inuyo zabwino simuzifuna Kodi ?

2025 timuke ndi THEME imeneyi Wishing you a happy blessed New year Mulungu amuke nanu nakupatsani zosowa zanu mu chaka c...
31/12/2024

2025 timuke ndi THEME imeneyi

Wishing you a happy blessed New year

Mulungu amuke nanu nakupatsani zosowa zanu mu chaka chimenechi

Tili ready ndithu
31/12/2024

Tili ready ndithu

Some of the selected pictures today
29/09/2024

Some of the selected pictures today

Its MASINTHA CCAP CHURCH CHOIRALBUM LAUNCH Live streaming mawa from BICC Inu Malo opita  mawa ndi ukuku Ndi 10,000 yokha...
28/09/2024

Its MASINTHA CCAP CHURCH CHOIR
ALBUM LAUNCH

Live streaming mawa from BICC

Inu Malo opita mawa ndi ukuku

Ndi 10,000 yokha basi inuyo mukanva mayimbidwe okoma ndi Ozuna

Tikakhala ife ma suit nde Ali ready ๐Ÿ˜

Big shout out to our newest top fans! ๐Ÿ’Ž Stellia Promise Lowe, Dรฃbรขby Black, Hawa Masakatira Mndala, Paul W***y Maganga, ...
20/09/2024

Big shout out to our newest top fans! ๐Ÿ’Ž Stellia Promise Lowe, Dรฃbรขby Black, Hawa Masakatira Mndala, Paul W***y Maganga, Pea Chago, Salome Ben, Lucy Chakwera, Martin Majomeka

We really appreciate your support ๐Ÿ™๐Ÿ™ month-end mumwa fanta ndithu ๐Ÿ˜๐Ÿ˜

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Masintha CCAP YOUTH Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share