Soul hunters international ministry - SHIM

Soul hunters international ministry - SHIM Hunting souls to Christ Jesus with Apostle Peter

Mawa itanani mzanu uja ndipo kabwereni naye limodzi.Mulungu sazakusiyani chimodzimodzi Mukhale ndi masana opambana tiona...
23/05/2026

Mawa itanani mzanu uja ndipo kabwereni naye limodzi.

Mulungu sazakusiyani chimodzimodzi
Mukhale ndi masana opambana tionane mawa ku church nthawi yabwino. Shalom🙏

Usiku wa lero ndikupemphera pa Altar yanga   mau ochokera kwa Mulungu kuti awuze anthu ako anene chomwe akufuna kuti chi...
19/05/2026

Usiku wa lero ndikupemphera pa Altar yanga mau ochokera kwa Mulungu kuti awuze anthu ako anene chomwe akufuna kuti chichitike pa moyo wawo chaka chino ndipo ine Mulungu wawo ndikwaniritsa angokhulupilira ( 11vs1)

what you want to do for you child of God🙏

Pakuti pamene awiri kapena atatu asonkhana pamodzi mʼdzina langa, Ine ndili nawo pomwepo.” Mateyu (18vs20)Kalikonse kame...
09/05/2026

Pakuti pamene awiri kapena atatu asonkhana pamodzi mʼdzina langa, Ine ndili nawo pomwepo.” Mateyu (18vs20)

Kalikonse kamene mtima wako ukhumbira ndikuti kachitike mwachangu motsogozedwa ndi mzimu oyera mu dzina la Yesu Christu !!!!🙏

This Thursday Midweek Service gonna be fire!! don't miss this, invite someone
06/05/2026

This Thursday Midweek Service gonna be fire!! don't miss this, invite someone

Pa mene talowa mwedzi uno wa May ndikulengeza chitetezo, machiritso, zisomo zochuluka ndi chipambano pa moyo wako komans...
02/05/2026

Pa mene talowa mwedzi uno wa May ndikulengeza chitetezo, machiritso, zisomo zochuluka ndi chipambano pa moyo wako komanso ma umboni ochuluka mu mwedzi uno wa May.

palibe chida chopangidwa ndi mdani chimene chidzakupweteke pa moyo wako( Yesaya 54vs17) Atero Yehova🙏

I am praying for you chatsopano chichitika pa moyo wako🤲
24/04/2026

I am praying for you chatsopano chichitika pa moyo wako🤲

Pakuti pamene awiri kapena atatu asonkhana pamodzi mʼdzina langa, Ine ndili nawo pomwepo.”Mulungu ali nanu kulikonse kom...
14/04/2026

Pakuti pamene awiri kapena atatu asonkhana pamodzi mʼdzina langa, Ine ndili nawo pomwepo.”

Mulungu ali nanu kulikonse komwe muyenda komanso pali ponse pomwe mugona masiku onse amoyo wanu. Ziki bwino ndi moyo wanu okhulupirira nonse ndikukudalitsani mu dzina la Yesu Christu🤲🙏

The grave is empty. what a great service it will be. come in good time join the teacher, the prophet, Apostle himself to...
04/04/2026

The grave is empty. what a great service it will be. come in good time join the teacher, the prophet, Apostle himself to make it short Join Eagle one.

Join us in Blantyre Soul Hunters Branch
01/04/2026

Join us in Blantyre Soul Hunters Branch

Today being Thursday we're having a great Midweek Service! you can't afford to miss this service! Soul hunters internati...
19/03/2026

Today being Thursday we're having a great Midweek Service! you can't afford to miss this service! Soul hunters international ministry - SHIM

Address

Area 21
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Soul hunters international ministry - SHIM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share