Heritage Sounds

Heritage Sounds We are a Christian Music singing group based at Monekera Central SDA church, Lilongwe Malawi.

We are a Christian music singing group based at Monekera Central SDA Church, Lilongwe, Malawi

Good night family and friends of Heritage Sounds
24/08/2026

Good night family and friends of Heritage Sounds

24/08/2026

‭EKSODO 25:8-9
[8] Ndipo andimangire malo opatulika; kuti ndikhale pakati pao. [9] Monga mwa zonse Ine ndilikuonetsa iwe, chifaniziro cha chihema, ndi chifaniziro cha zipangizo zake zonse, momwemo uchimange.

24/08/2026

Kuli bwanji kwathu?

Khristu Mu Nyimbo Number 5

Get ready for a big day at Chisiyo SDA church to be hosted by the best communicator, Samson Naziri,  and music by Acca F...
24/08/2026

Get ready for a big day at Chisiyo SDA church to be hosted by the best communicator, Samson Naziri, and music by Acca For Him

  bwanji Amzathu. Tiyeni tiyambe tsiku lathu ndikupereka nkhawa zathu zonse Kwa Yesu. ‭MATEYU 11:28Idzani kuno kwa Ine n...
24/08/2026

bwanji Amzathu. Tiyeni tiyambe tsiku lathu ndikupereka nkhawa zathu zonse Kwa Yesu.

‭MATEYU 11:28
Idzani kuno kwa Ine nonsenu akulema ndi kuthodwa, ndipo Ine ndidzakupumulitsani inu.

Few days to the Chilinde District Camp Meeting. Tiyeni tiyambepo kukomzekera.
23/08/2026

Few days to the Chilinde District Camp Meeting. Tiyeni tiyambepo kukomzekera.

Kodi ndi nyimbo iti imene imakusangalatsani and imakusangalatsani chifukwa chiyani?
23/08/2026

Kodi ndi nyimbo iti imene imakusangalatsani and imakusangalatsani chifukwa chiyani?

Congratulations to Master Guide Hakainde HiChilema on your re-election! 🎉👏Your leadership, dedication, and service conti...
23/08/2026

Congratulations to Master Guide Hakainde HiChilema on your re-election! 🎉👏

Your leadership, dedication, and service continue to inspire. May God grant you wisdom and strength for the journey ahead. 🙏🏽✨

Congratulations, Master Guide! 🫡🔥

All is set for the Peculiar Music Ministries album launch. Kodi Inu Ticket mwaipeza kale?
23/08/2026

All is set for the Peculiar Music Ministries album launch. Kodi Inu Ticket mwaipeza kale?

‭YOHANE 14:23Yesu anayankha nati kwa iye, Ngati wina akonda Ine, adzasunga mau anga; ndipo Atate wanga adzamkonda, ndipo...
23/08/2026

‭YOHANE 14:23
Yesu anayankha nati kwa iye, Ngati wina akonda Ine, adzasunga mau anga; ndipo Atate wanga adzamkonda, ndipo tidzadza kwa iye, ndipo tidzayesa kwa iye mokhalamo.

Address

Monekera Central SDA Church, Area 21 Chilinde
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Heritage Sounds posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share