Msunga CCAP Nkhoma SYNOD

Msunga CCAP Nkhoma SYNOD MSUNGA CCAP is a church under Nkhoma Synod and is situated in Chinsapo 1 (Area 57). The church minister is Reverend TAD JUMA PHIRI

MSUNGA CCAP is a church under Nkhoma Synod and is situated in Chinsapo 1 (Area 57), Lilongwe.

26/08/2026

Mwambo wa Maliro Opelekeza thupi la Bambo

25/08/2026

Achinyamata Kodi Mwakonzeka!!!!!!!?????🗣️🗣️🗣️🗣️🗣️🗣️
Mwachapa kale Black ndi White wanu? Nanga zofunda?
pajatu ndipa 27 August, Lachinayi lino ku Likuni CCAP
Osaiwala Baibulo, Buku la Nyimbo, komanso Polemba.
Zambili Onerani Kanemayu.
Likuni Presbytery Ccap Youth

21/08/2026

Takulandilani Ku Mwambo Operekeza Thupi La Bambo Cosmas Chibwe
BORN: 01 OCT 1956
DIED: 20 AUG 2026
BURRIED: 21 AUG 2026

18/08/2026

Kodi Chikondi Cheni cheni ndi chiti?

16/08/2026

Takulandirani Ku Chipembedzo Cha Lero Cha Chichewa.
Olalikira: Abusa T.A.D. Juma Phiri

13/08/2026

Ona chisangalalo iweee🙌

As Malawi Celebrates Women's qualification in the WAFCON finals, nawo Amayi ochokera mu Likuni Presbytery ayamba kale kuvina ndi kukondwera pokondwera ulendo wa msonkhano wa Women's Guild 2026.

Mutu: "Funa mtendere ndikuulondola"

Ngati simunayambe kukonzeka, tsopano ndi nthawi! Nyamulani zikwama zanu, zovala za Guild, ndi mtima wokonzeka kulandira madalitso.

Tikukumana ku Katate! 🔵



!!!

Last Sunday's Joint Service in pictures.A very big shout-out to the defending Champions, Station 3 in last Sunday's Big ...
04/08/2026

Last Sunday's Joint Service in pictures.

A very big shout-out to the defending Champions, Station 3 in last Sunday's Big Paper.

To our newly inducted Men's Guild members, welcome. May God use you Mightly.


01/08/2026

Takulandirani Ku Mwambo Opelekeza Thupi La Mayi Eneless Kandodo Moyo.
BORN: 06 JULY 1969
DIED: 30 JULY 2026
BURIED: 01 AUG 2026
MAY HER SOUL REST IN PEACE

30/07/2026

Day 29 of 30 days of breaking the spirit of Stagnation and Delay.
Preacher: Mr L. Kadumbo

Address

MSUNGA CCAP
Lilongwe
XPQM+773

Telephone

+265998205019

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Msunga CCAP Nkhoma SYNOD posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Msunga CCAP Nkhoma SYNOD:

Shortcuts

Share

Category