Zolozolo S.D.B church

Zolozolo S.D.B church Zolozolo is a branch under mzuzu joint in the northern association of the CAC of SDB

01/07/2023

I welcome you back all. it has been a long time since i visited this page but now i can confirm that the page will be active to give SDB members updates on church developments and other ministerial programs. thanks

Ena mwa zibusa anthu akuno kumpoto
01/11/2021

Ena mwa zibusa anthu akuno kumpoto

22/10/2021

Tili ndi youth camp kuno ku mzuzu joint imene izayamba pa 28th november mpaka pa 4 December ndipo ikachitikile ku Enyezini pa CDSS. Tiyeni tizikonzekera anyimata kuti tikafalitse uthenga wa ambuye wathu yesu khristu

18/06/2021

Takulandirani nonse pano page lathu la Zolozolo SDB church. Mpingo umenewu ukupezekera chigawo chakumpoto mumzinda wa Mzuzu pafupi ndi zolozolo CCAP church m'mbali mwamsewu opita Ku Mzuzu technical college. Timasangalala kwambiri ndi alendo obwera kuzatichezera khalani omasuka ndithu. Amen!!!

Address

Zolozolo SDB Church, Box 161, Mzuzu
Lilongwe

Telephone

+265888591159

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zolozolo S.D.B church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Zolozolo S.D.B church:

Share

Category