Kingdom Ambassadors lnternational Church

Kingdom Ambassadors lnternational Church A church that is determined to preach the Gospel of God to the World.

FAMILY DELIVERANCE,  Mawa tikupempherera mamasulidwe a banja lakwanu lonse, kusatengera kuti zinthu zako zikuyenda koma ...
23/05/2026

FAMILY DELIVERANCE,

Mawa tikupempherera mamasulidwe a banja lakwanu lonse, kusatengera kuti zinthu zako zikuyenda koma ngati achibale akuvutika mtendere sumakhala nawo! Mawa Mulungu wakonzeka kumasula banja lakwanu lonse!

ZONSE ndizotheka ndi Ambuye ❗️

Saturday linali tsiku lopambana pamene tinapita kukalalilira uthenga wabwino mumadera osiyanasiyana mmuzinda wa Blantyre...
20/05/2026

Saturday linali tsiku lopambana pamene tinapita kukalalilira uthenga wabwino mumadera osiyanasiyana mmuzinda wa Blantyre!

Anthu ochuluka alandira Yesu kukhala mbuye ndimpulumutsi wamoyo wawo! Pamene ife timasangalala kuti takwanitsa zaka 5 kumwamba nakoso kumasangalala chifukwa anthu amene apulumutsidwa atamvera utheka wabwino!

PEMPHERO LANGA ndilakuti Yesu Khristu apulumutse banja lakwanu lonse!

Mawalimo tikumarizitsa zokondwerera zonse kuti utumiki wathu wakwanitsa zaka zisanu ( 5th Church anniversary) service ik...
16/05/2026

Mawalimo tikumarizitsa zokondwerera zonse kuti utumiki wathu wakwanitsa zaka zisanu ( 5th Church anniversary) service ikudzayamba 8 - 11Am.

Zikondwerero ndimadyerero zikudzayamba 1- 5PM.

Musadzabwere ndizakumwa Komaso zakudya zonse mudzazipeza konkuno😂🔥!!

Nonse militants‼️

PAMENE tikukumbukira kuti utumiki wakwanitsa zaka 5, mawalino tikhala tikupita mumisewu ndi malo osiyanasiyana a mmuzind...
15/05/2026

PAMENE tikukumbukira kuti utumiki wakwanitsa zaka 5, mawalino tikhala tikupita mumisewu ndi malo osiyanasiyana a mmuzinda wa Blantyre. Ndi nthawi yabwino yomufikira wina ndiuthenga wabwino!

YESU akubwera posachedwa!

TOMORROW we’re hitting the streets of Blantyre with the gospel of our Lord Jesus Christ!

SUNDAY tinali ndi service yopambana, kwathu ndikuthokoza Ambuye kamba ka chisomo chawo pa ife!PEMPHERO langa ndilakuti A...
14/05/2026

SUNDAY tinali ndi service yopambana, kwathu ndikuthokoza Ambuye kamba ka chisomo chawo pa ife!

PEMPHERO langa ndilakuti Ambuye APITILIZE KUCHITA NANU, mudzina la Yesu khristu ‼️

This week is a very special week to me, my wife, and the entire Kingdom Ambassadors International Church because this is...
12/05/2026

This week is a very special week to me, my wife, and the entire Kingdom Ambassadors International Church because this is the week we’re celebrating our 5th Church Anniversary. God has been faithful to us throughout all these past 5 years because He has helped us conquer everything the enemy brought our way to stop us. Like any other vision, we had our ups and downs, but God’s grace, mercy, and power have brought us this far. Looking at how many souls are being blessed through this ministry is a very humbling thing — a true testament of the grace of God!

All we can say is EBENEZER! And many more years to come! Happy 5th anniversary to KAIC!!!!!

Tikumane ku Church mawa, Ambuye alinanu mau. Service ikudzayamba 8Am Sharp.BROKEN TO STAND!
09/05/2026

Tikumane ku Church mawa, Ambuye alinanu mau. Service ikudzayamba 8Am Sharp.

BROKEN TO STAND!

SUNDAY was amazing!Lero mukuitanidwa ku MIDWEEK SERVICE masana ano! Service imayamba 2Pm kulekeza 5:30Pm.ZAMPHAMVU ZIKUC...
07/05/2026

SUNDAY was amazing!

Lero mukuitanidwa ku MIDWEEK SERVICE masana ano! Service imayamba 2Pm kulekeza 5:30Pm.

ZAMPHAMVU ZIKUCHITIKA‼️

Address

Kanjedza

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 18:00
Friday 09:00 - 18:00
Saturday 09:00 - 18:00
Sunday 09:00 - 17:00

Telephone

+265993669700

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kingdom Ambassadors lnternational Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Kingdom Ambassadors lnternational Church:

Share