04/09/2026
ZILIBWINO
Luka 1:37
Cifukwa palibe mau amodzi akucokera kwa Mulungu adzakhala opanda mphamvu
Ukamva mphamvu zatha ndipo ukufuna kusiya, yesanso kamodzi. Nthawi zambiri kupambana kumakhala pa kuyesa komaliza.
Mwezi uno wa September,Yehova Mulungu asegule makomo akukondeledwa pamoyo wanu.
Mu Dzina la Yesu