Apostle Daniel Masina

Apostle Daniel Masina The founder of Jerusalem foundation of christ..
(1)

03/06/2026

Tsiku lina udzalira misozi osati chifukwa chak*ti wina wake wakukhumudwitsa koma k*t Mulungu wayakha mapemphero ako.

๐Ÿ™๐ŸŽ‰Happy birthday to my spiritual dad! Ndi madalitso akulu kukhala ndi bambo wauzimu amene amakulangiza, amakupemphera, n...
03/06/2026

๐Ÿ™๐ŸŽ‰

Happy birthday to my spiritual dad! Ndi madalitso akulu kukhala ndi bambo wauzimu amene amakulangiza, amakupemphera, ndi kukusonyeza njira ya Mulungu.

Happy birthday Dear Dad. Thank you for your guidance, wisdom, and prayers. May God continue to bless you with good health, peace, and joy. We love and honor you.

Dear Dad,
Lero tikukondwerera moyo wanu. Zikomo chifukwa cha uphungu, nzeru, ndi chikondi cha uzimu chimene mumatipatsa. Mulungu akudalitseni ndi mphamvu, mtendere, ndi chisangalalo tsiku ndi tsiku. Tikupempha k*ti ulendo wanu wauzimu upitirire kudzazidwa ndi chisangalalo, chikondi, ndi kuunikira kwa Mulungu.
Happy birthday ndipo Mulungu akudalitseni kwambiri.

[ TIPEMPHERE๐Ÿ™‡๐Ÿปโ€โ™‚๏ธ ]Atate mudzina lamphamvu la Ambuye wathu Yesu Khrist,Mutamandike mulemekezeke Inu Yehova Mulungu wathu...
03/06/2026

[ TIPEMPHERE๐Ÿ™‡๐Ÿปโ€โ™‚๏ธ ]

Atate mudzina lamphamvu la Ambuye wathu Yesu Khrist,

Mutamandike mulemekezeke Inu Yehova Mulungu wathu wamakamu,

Zikomo Yehova Mulungu wakumwamba-mwamba kamba kachikondi chanu komaso chifundo chanu Ambuye,

Tikuyamikani komaso kuk*thokozani Ambuye k*ti mwatidzutsaso ndi moyo,

Tikudziwa Ambuye k*ti Inu pamene mwatidzutsa ndi moyo alipo ena sadadzike,

Inde kugona komweku kwa watengera imfa,

Ife popezeka ndi moyo zatengera chisomo ndi mphamvu zanu inde kukoma mtima kwanu Ambuye,

Tikupemphani Yehova mukhale nafe ndik*titsogolera mtsiku ili,

Mutitalikitse k*tali ndi machita-chita a Satana inde ngakhale makhalidwe akudziko lapansili

Tipemphera azanu onse omwe tili ku south africa ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ k*t Mulungu awateteze ndikuwaphimba ndi dzanja lake .

Odwala thenda zosiyana-siyana Ambuye muwakumbukire ndikuwakhudza ndi dzanja lanu lamphamvu la machiritso k*ti;

Achiritsidwe ndikumasulidwa mudzina la Yesu khristu Ndapemphera ndimokukhulupirirani komaso kukudalirani Amen๐Ÿ™.

02/06/2026

Mulungu wathu amapereka kwa ana zithu zoyenera ..

02/06/2026

PEMPHERO LOGONERA
Mphamvu zakumdima zomwe zimadyesa anthu k*tulo Poison!Usikuno tikuziononga Mzina la mphamvu la Yesu khrist๐Ÿ•Š๏ธ๐Ÿ”ฅ

Ndikupemphera k*ti mwezi uno wa June aliyese onenelera moyo wako k*ti usazapindule uzingovutika,nyengo zako zizingolimba...
02/06/2026

Ndikupemphera k*ti mwezi uno wa June aliyese onenelera moyo wako k*ti usazapindule uzingovutika,nyengo zako zizingolimba Mulungu achite naye.Zonse zomwe anayankhula paiwe ndikuzithetsa mdzina laYesu.Zonse zibwelere kwa eni ake.Maguwa awo omwe amanenelerapo zoipazo agwe, Mphamvu zawo zithe ndipo kuyambira lero chatsopano mwaiwe chiyambe kuoneka mdzina la Yesu ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

02/06/2026

๏ธ๐Ÿ•Š
MULUNGU akupatseni CHISOMO CHOCHULUKA pa moyo wanu ndipo mbiri yanu isinthe ndi ma umboni ochuluka..

01/06/2026

Pempherani pamene zithu zikuyenda bwino, pempherani pamene zithu zisakuyenda bwino. Pempherani kosalekeza

01/06/2026

Mwez uno wa June Mulungu akupase ntchito yabwino,akuze business yako,ak*teteze kungozi ndi imfa mu dzina la yesu khristu.Amen

Ambuye ndikukupemphani k*ti nzanga akuwerengayu mumudalitse mu mwezi uno wa June mnyumba mwake musasowe kanthu, Minyama,...
01/06/2026

Ambuye ndikukupemphani k*ti nzanga akuwerengayu mumudalitse mu mwezi uno wa June mnyumba mwake musasowe kanthu,

Minyama, matsoka, nthenda, imfa, zikhale k*tali ndi moyo wake Mudzina la Yesu nkhristu ๐Ÿ™๐Ÿ™

Address

George Western Cape, Thembalethu Zone 9
George

Telephone

+27814359233

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Apostle Daniel Masina posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Apostle Daniel Masina:

Share