Mpesa Durban SDA. Church _Malawians.

Mpesa Durban SDA. Church _Malawians. Is Malawian Church in Durban South Africa, that does the services in Chichewa language or in other cases , been interpreted in Chichewa.

Mapempheredwe a Chichewa ku Durban South Africa SDA.

09/09/2026

SHOWERS OF BLESSINGS _ MLENDO WATHU

09/09/2026

MLENDO WATHU:

MVERANI PROGRAM YA MLENDO WATHU KUCHOKERA KU MPESA MEDIA.

MU PROGRAM YA LERO, MUMVERA MTOLANKHANI WATHU GIFT MAMBUCHA BANDA AKUCHEZA NDI GULU LOYIMBA LA;

SHOWERS OF BLESSINGS

DALITSIKANI !!

09/09/2026
MLENDO WATHUMVERANI PROGRAM YA MLENDO WATHU  LERO NTHAWI YA  6:00 MADZULO PA MPESA SDA CHURCH  WHATSAPP KOMANSO FACEBOOK...
09/07/2026

MLENDO WATHU

MVERANI PROGRAM YA MLENDO WATHU LERO NTHAWI YA 6:00 MADZULO
PA MPESA SDA CHURCH WHATSAPP KOMANSO FACEBOOK PAGE NDI GROUP

MTOLANKHANI WATHU WA MPESA MEDIA AKHALA AKUCHEZA NDI GULU LOYIMBA NYIMBO ZA UZIMU LA:

PHILADELPHIA SINGERS MW

MUSATALIKILE KUTI MUMVE NDI KUPHUNZIRA ZAMBIRI !!

02/07/2026

MPESA MEDIA TIKUPATSILANI PROGRAM YA:

MLENDO WATHU.

Ndipo mu program ya lero mumvera MTOLANKHANI WATHU DANIEL SOLOBENI akucheza ndi Woyimba nyimbo za Uzimu,
DORIS KANYANG'AMA.

TIYENI TIMVETSERENI LIMODZI !!

Address

30 Field Street, , Kings Field Building, , Floor Number 4
Durban

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mpesa Durban SDA. Church _Malawians. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share