Mchezi CCAP Church

Mchezi CCAP Church Mchezi CCAP Church is situated in Area 27, Lilongwe

Nthuni Mwadzukako bwanji tsiku la lero?Paper Sunday ijatu ndi leroTiyeni tiyeni ndithuNdipo osafooka...chikho 🏆tikachite...
07/06/2026

Nthuni

Mwadzukako bwanji tsiku la lero?

Paper Sunday ijatu ndi lero
Tiyeni tiyeni ndithu
Ndipo osafooka...chikho 🏆tikachitenge

Mchezi CCAP Church

01/06/2026

Abale okondedwa mwa Ambuye.
Mukhale ndi mwezi watsopano (June) opambana

Mchezi CCAP Church

Nthuni lero ndi tsiku lomaliza la sabata  la mwezi wa Meyi m'chaka cha 2026.Zambiri zabwino komanso zoipa zachitika mmwe...
31/05/2026

Nthuni lero ndi tsiku lomaliza la sabata la mwezi wa Meyi m'chaka cha 2026.

Zambiri zabwino komanso zoipa zachitika mmwezi umenewu. Kukhalabe ndi moyo pofika lero zatengera chisomo ndi chikondi chake. Choncho zifukwa zathu ndi zochuluka kumuimbira/kumupembedza Mulungu wathu. Watitetezera ku misampha yoopsa ya mitundu yosiyanasiyana.

Ife ndi ndani kuti tisamuyamike IYE?

Mchezi CCAP Church

Happy Ascension day fellow worshipersActs 01 vs 6 - 9Mchezi CCAP Church
24/05/2026

Happy Ascension day fellow worshipers

Acts 01 vs 6 - 9

Mchezi CCAP Church

JOIN US TODAY FORPENTECOST BLOCK WEEK SERVICETHEME : KUZINDIKIRA MZIMU OYERA NDI NTCHITO ZAKE                (YOHANE 14 ...
19/05/2026

JOIN US TODAY FOR
PENTECOST BLOCK WEEK SERVICE

THEME : KUZINDIKIRA MZIMU OYERA NDI NTCHITO ZAKE
(YOHANE 14 VS 26)





Mchezi CCAP Church

10/05/2026

Good morning our beloved followers.

May the good Lord hear your cry and answer you in the right time.

Mchezi CCAP Church
Lolani Chikondi Chitsogolere.

Nthuni lero ndi tsiku linanso la mtengo wapatali....Tiyeni tikapemphere....Nyengo zolimbazo mayankho ake ndiko kupempher...
19/04/2026

Nthuni lero ndi tsiku linanso la mtengo wapatali....

Tiyeni tikapemphere....

Nyengo zolimbazo mayankho ake ndiko kupemphera

Mukhale ndi tsiku lopambana

Mchezi CCAP Church

We've just reached 300 followers! Thank you for continuing support. we could never have made it without each one of you....
16/04/2026

We've just reached 300 followers! Thank you for continuing support. we could never have made it without each one of you. 🙏🤗🎉

Follow
Mchezi CCAP Church

06/04/2026

Nanga lero mwadzukako bwanji?

Follow
Mchezi CCAP Church

Address

Area 27
Lilongwe

Opening Hours

Monday 07:00 - 19:00
Tuesday 07:00 - 19:00
Wednesday 07:00 - 19:00
Thursday 07:00 - 19:00
Friday 07:00 - 19:00
Saturday 07:00 - 19:00
Sunday 07:00 - 19:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mchezi CCAP Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category