Msamba Catholic Parish

Msamba Catholic Parish We are a parish in the Archdiocese of Lilongwe, Malawi, located in Area 36 in the southern part of the capital. Established as a parish in 1984, St.

John the Baptist –Msamba– Parish is under Comboni Missionaries (MCCJ) and oversees 6 church stations.

Bwerani pafupi ndi Mulungu ndikutula mayamiko kapena nkhawa zanu kudzera kwa Ambuye Yesu M'sakramenti la Ukaristia. Lach...
13/08/2026

Bwerani pafupi ndi Mulungu ndikutula mayamiko kapena nkhawa zanu kudzera kwa Ambuye Yesu M'sakramenti la Ukaristia. Lachinayi lirilonse nthawi ya 4 koloko masana, ku Msamba.

Chimwemwe chathu ku Msamba chikupitilira pamene Bambo Peter Kelvin Makina tsopano atsankhidwa kukhala Mlembi wa Akiepisk...
29/07/2026

Chimwemwe chathu ku Msamba chikupitilira pamene Bambo Peter Kelvin Makina tsopano atsankhidwa kukhala Mlembi wa Akiepiskopi wa Lilongwe kuyambira mwezi wa July 2026. Tiyeni tiwafunire zabwino zonse.

Happy Anniversary Fr Jean Marie.
22/07/2026

Happy Anniversary Fr Jean Marie.

27/06/2026

Nawo a zida kuchipatsa Chaka cha Yohane M:batizi Woyera moto.

27/06/2026

Mdipiti kukalowa tsopano

Address

Area 36
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Msamba Catholic Parish posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share