St Bernadette Catholic Choir Capetown

St Bernadette Catholic Choir Capetown Our lives will be a continuous melody sung in praise to God.

Mwapita koma sitidzaiwala izi..Muyende bwino abale..TIKUTHOKOZENI KWA NONSE AMENE MUNADZATIKUTA PA MWAMBO UWU..IFEYO TIK...
07/09/2026

Mwapita koma sitidzaiwala izi..
Muyende bwino abale..
TIKUTHOKOZENI KWA NONSE AMENE MUNADZATIKUTA PA MWAMBO UWU..
IFEYO TIKUTI ZIKOMO KWAMBIRI PAIFE TOKHA ZIKADATIKULIRA πŸ™

06/09/2026

Mwambo otsazikana ndi abale athu
Pozzy P Kalilombe
Clara Kazembe Bulozi
πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ•Š

🚨Pamene tikupitilira kulira abale athu awiriwa.Mawa ndi tsiku lomwe tikutsanzikana nawo  komasoPozzy P Kalilombe ku St A...
05/09/2026

🚨Pamene tikupitilira kulira abale athu awiriwa.
Mawa ndi tsiku lomwe tikutsanzikana nawo
komaso
Pozzy P Kalilombe ku St Annie's Catholic Hall Capetown.
Mwambo udzayamba 11 O'clock m'mawa ,ndipo uku amasunga nthawi.
Dzafikeni mwachangu kuti mwambowu tidzayambire limodzi.
"CLARA KAZEMBE BULOZI" Adatisiya lachitatu pa 29th August atachita ngozi mu njanji ya train.
Patadutsa masiku atatu ndipamene Kalilombe amatisiyaso lomwe lidali pa 2 September atangoti ndikumva chizungulire adagwa pompo ndikumwalira.

Dziwani kuti ili silidali banja zidangochitika kuti adatisiya
Week imodzi motsatizana
Mphakati umodzi wa St Pius
Church cha St Bernadette Catholic,Capricorn, Capetown..
Onsewa amachokera ku Blantyre chakuchileka.

Mizimu ya abale athuwa ikawuse mumtendere..πŸ•ŠπŸ•ŠπŸ•ŠπŸš¨

https://maps.app.goo.gl/iXSvH1aG1c6bHTYG8

31/08/2026

Mwambo ukupitilira olira abale athu awiri...
Tikumasonkhana ku Catholic Church Capricorn
Nthawi ya 5:30.

🚨Tidzikhala okonzeka abale..Nthawi sikutidikira..πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”Ifeyo chonena tilibe 😭😭😭😭😭🚨
30/08/2026

🚨Tidzikhala okonzeka abale..
Nthawi sikutidikira..
πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”
Ifeyo chonena tilibe 😭😭😭😭😭🚨

Ku St Bernadette Church sizikutichoka.Tili mkati molira Zina zatipezaso..Tilire bwanji? Nyengo yowawa kwambiri..M'mawa w...
30/08/2026

Ku St Bernadette Church sizikutichoka.
Tili mkati molira
Zina zatipezaso..Tilire bwanji?
Nyengo yowawa kwambiri..

M'mawa walelo wangoti chizungulire ndikugwa basitu imfa ndi yomweyo.
Zachitika muma seconds. πŸ’”πŸ’”πŸ•Š
Pozzy P Kalilombe

🚨Zosayenda ku mpingo kwathu Pomwe dzulo m'bale wathu amene timasonkhana naye limodziSt Bernadette Church Capetown watisi...
27/08/2026

🚨Zosayenda ku mpingo kwathu
Pomwe dzulo m'bale wathu amene timasonkhana naye limodzi
St Bernadette Church Capetown watisiya..
Muyende bwino Sister..πŸ’”πŸ•ŠπŸš¨

Hello πŸ‘‹ Family Help to celebrate the birthday of our our member Enjoy your day Abiti
06/08/2026

Hello πŸ‘‹ Family
Help to celebrate the birthday of our our member
Enjoy your day Abiti

OOODIIIIIII KUMENEKO IFE A KU BANJA LA  ST BERNADETTE CHOIR TIKUKONDWELELA KUBADWA KWA MEMBER WATHU KOMASO KEYBOARDIST W...
29/07/2026

OOODIIIIIII KUMENEKO IFE A KU BANJA LA ST BERNADETTE CHOIR TIKUKONDWELELA KUBADWA KWA MEMBER WATHU KOMASO KEYBOARDIST WATHU YEMWE WAWONJEZELA CHAKA CHINA.TITHANDIZENI KUSANGALALA NAFE POMWE TIKUKONDWELELA .IFE TIGOTI HAPPY BIRTHDAY SIR ,PITILIZANI KUKHALA MUNTHU ODZICHEPESA KOMASO OKONDA CHOIR YANU πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³HAPPY HAPPY BIRTHDAY MAY GOD CONTINUE GIVE YOU A GOOD LIFEπŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³

Taweluka
16/07/2026

Taweluka

Address

25 Fredrick Road Vrygrond
Cape Town

Opening Hours

Tuesday 17:00 - 18:40
Thursday 17:00 - 18:40
Saturday 16:00 - 18:00
Sunday 08:30 - 11:00

Telephone

+27630304052

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when St Bernadette Catholic Choir Capetown posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share