Seventh-day Adventist Church- Kamuzu Road

Seventh-day Adventist Church- Kamuzu Road Tsambali ndi la Mpingo wa Seventhday Adventist ku Kamuzu Road boma la Salima

29/08/2026

Sabbath Photos πŸ˜ŠπŸ“ΈπŸ€³

Pamene tikukonzekera Camp Meeting ya Chaka Chino tiyeni tioneko za mchaka cha 2019.Camp meeting ya m'chaka cha 2019 inac...
29/08/2026

Pamene tikukonzekera Camp Meeting ya Chaka Chino tiyeni tioneko za mchaka cha 2019.

Camp meeting ya m'chaka cha 2019 inachitikira Ku Senegabay SDA ndipo amatsogolera chilinganizo cha Masana anali Adventist Men Organization (AMO).

Mafunso.
1. Kodi Gulu loimba lomwe lomwe linaitanidwa kuzatumikira linali lochokera kuti? Tchulani dzina la Gulululo.

2. Ma Chair a Chilinganizochi anali ndani? - (Hint: Mmodzi mwa ma Chair-wa anali ochokera pa Kamuzu Road πŸ˜€)

Pelekani mayankho anu mu comment section.

Seventh day adventist Chitala church
Seventh-day Adventist Church - Lipimbi
Seventh-day Adventist Church- Kamuzu Road
fans

29/08/2026

Devine Service Segment;

Chair: Mr T. Chirwa

First Prayer: Luke Vitola

Preacher: Shepherdess Mtiyesanji

Second Prayer: Mr Y. Mphanga

Chorister: Miss Norcia Zilosi

Singing Group: Dorcas

29/08/2026
29/08/2026

Mwaloweza kale nyimbo ya Misasa? πŸ˜€
Lero bwerani Ku church nthawi yabwino tiphunzire nyimbo ya Msasa komaliza.
.

KAMUZU ROAD YOUNG DORCAS Seventh day adventist Chitala church Seventh-day Adventist Church - Lipimbi Mtakataka District of the Seventh-day Adventist Church

Yankho la funso lomwe tinafunsa masiku awiri apitawo..Kodi OneVoice27 ndi Chiyani? πŸ‘‡πŸ‘‡Pitilizani kutsatira tsamba lino ko...
29/08/2026

Yankho la funso lomwe tinafunsa masiku awiri apitawo..
Kodi OneVoice27 ndi Chiyani? πŸ‘‡πŸ‘‡

Pitilizani kutsatira tsamba lino komanso pangani share Kwa anzanu kuti tiphunzire zambiri.

Wishing you all a blessed Sabbath.Meet you on 6th Sept at Kamuzu Road Church for the 2026 Annual Camp meeting! KAMUZU RO...
28/08/2026

Wishing you all a blessed Sabbath.
Meet you on 6th Sept at Kamuzu Road Church for the 2026 Annual Camp meeting!

KAMUZU ROAD YOUNG DORCAS Salima Central SDA Church Seventh-day Adventist Church - Lipimbi Seventh day adventist Chitala church Mtakataka District of the Seventh-day Adventist Church Central Malawi Conference of SDA Church

Masiku ambuyomo...  fans
27/08/2026

Masiku ambuyomo...

fans

Counting down! 30th August for Michael Blackand Talandira πŸ€—πŸ₯³
27/08/2026

Counting down!
30th August for Michael Blackand Talandira πŸ€—πŸ₯³

Pa 30 Ogasite pano aliyense kopita akukudziwa. πŸ€—πŸ₯³πŸ₯³
Mpunga ya nyamaπŸ˜‹
fans

❓ Question Time! Let's see who knows this mission!Q: What is One Voice 27? πŸ€”Drop your answers in the comments box below!...
27/08/2026

❓ Question Time!

Let's see who knows this mission!

Q: What is One Voice 27? πŸ€”
Drop your answers in the comments box below! πŸ‘‡
We are officially calling on Chikondi Jamali Chancy KachiwalaMuwama Aggrey ChirwaKASA GRAPHICSMpha Sonia ChungaJustin Missi Michael Black Wisok Sosola to give us their best answers!

πŸ”„ Keep the chain going: Once you comment, tag someone you know who needs to learn about this mission, and challenge them to do the same!

Address

Off Kamuzu Road
Salima

Telephone

+265888179602

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Seventh-day Adventist Church- Kamuzu Road posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share