Church of Central Africa Presbyterian- CCAP Traveller

Church of Central Africa Presbyterian- CCAP Traveller This page is dedicated to sharing the history, doctrine, worship practices, and community work of CCAP particularly in Malawi.

Stay tuned as we explore the rich heritage and spiritual depth of one of Africa's most vibrant Christian religionπŸ™πŸ™

15/08/2026

Hello saints 😊

Tili busy 😊😊
15/08/2026

Tili busy 😊😊

We thank God πŸ™πŸ™. After a setback of vandalism which happened some year back,  Robert Blake is back to its best. Today we...
15/08/2026

We thank God πŸ™πŸ™. After a setback of vandalism which happened some year back, Robert Blake is back to its best. Today we celebrate that the school is among top ten best performing schools for the released JCE results.

TSIKU LA 227  MU CHAKA CHA 2026. (15/08/26). ‼️ MAWU OPATSA MOYO ‼️ πŸ™πŸ™ Yobu 8:7 "Chiyambi chako chidzaoneka ngati choche...
15/08/2026

TSIKU LA 227 MU CHAKA CHA 2026. (15/08/26).

‼️ MAWU OPATSA MOYO ‼️ πŸ™πŸ™

Yobu 8:7

"Chiyambi chako chidzaoneka ngati chochepa, koma chimaliziro chako chidzakula kwambiri"

Phunziro:

Zimene tikukumana nazo panopa sizitanthauza tsogolo lathu lidzakhalaso chomcho. Mulungu adzatitsogolera ku chipambano ndipo tidzafika patali ngati tipitiriza kumukhulupirira ndi kudalira Iye mu zonse.πŸ‘πŸ‘

Goodmorning saints 😊

Tiyeni πŸ₯³
14/08/2026

Tiyeni πŸ₯³

14/08/2026

Goodmorning saints πŸ˜ŠπŸ™

TSIKU LA 226  MU CHAKA CHA 2026. (14/08/26). ‼️ MAWU OPATSA MOYO ‼️ πŸ™ Yohane 4:23 "Koma ikudza nthawi, ndipo tsopano ili...
14/08/2026

TSIKU LA 226 MU CHAKA CHA 2026. (14/08/26).

‼️ MAWU OPATSA MOYO ‼️ πŸ™

Yohane 4:23

"Koma ikudza nthawi, ndipo tsopano ilipo, imene olambira oona adzalambira Atate mumzimu ndi m'choonadi; pakuti Atate afuna otere akhale olambira ake."

Phunziro:

Mulungu akufuna anthu amene azimulambira m***a mtima. IYE sakufuna kumulambira ndi mawu kapena zochita zakunja zokha, koma ndi mtima weniweni (wokhazikika mu choonadi), motsogozedwa ndi Mzimu Woyera. πŸ‘πŸ‘

Goodmorning saints 😊

Kabwelani ndithu πŸ₯³πŸ₯³
13/08/2026

Kabwelani ndithu πŸ₯³πŸ₯³

The vision is on, God will make it into reality πŸ™ Tiyeni tithandize madodana pamsi pa Livingstonia synod kumanga ofesi z...
13/08/2026

The vision is on, God will make it into reality πŸ™

Tiyeni tithandize madodana pamsi pa Livingstonia synod kumanga ofesi zawo. Ofuna kuthandiza kapena kumva zambiri gwiritsani ntchito ma account number komaso contact number ziri mu poster pamsipa.

Synod πŸ–€πŸ€

13/08/2026

Ena lero mukuuyamba msonkhano wa amayi wapachaka. Zabwino zonse!!!

Address

Salima

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Church of Central Africa Presbyterian- CCAP Traveller posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share