Police Headquarters CCAP

Police Headquarters CCAP BISWICK CHIMBALU NKHOMA.

POLICE HEADQUARTERS CCAP" is a Christian Church under The CCAP General assembly, inaugurated on "6th November 2022" by the moderator of The CCAP General assembly Rev.

Ana anu kapena ana akwanu amapemphera inuyo??? Mumawatumiza ku Sunday school inuyo ?? Kapena munawatumiza koma iwowo sam...
30/08/2026

Ana anu kapena ana akwanu amapemphera inuyo??? Mumawatumiza ku Sunday school inuyo ?? Kapena munawatumiza koma iwowo samabwera? Iyayi similandu ndangokufusan ine

Here are photos we captured at Sunday school today

komaso k*tola zinthunzi ndi Fraser D. Phiri

Police Headquarters CCAP

Uthenga wa chisoni: Mai awo akulu a akulu a mpingo mai B. Munthali a ku 30A atisiya ku Kamuzu Central hospital ndipo mal...
28/08/2026

Uthenga wa chisoni:

Mai awo akulu a akulu a mpingo mai B. Munthali a ku 30A atisiya ku Kamuzu Central hospital ndipo maliro anyamuka mawa kupita ku Rumphi komwe akaikidwe lolemba pa 31 August, 2026.

Tiyeni tiwaikize mu mapemphero k*ti ayende bwino komanso mwambo onse ukayende bwino.

Khaaaaaaa another birthday lero Kuchokera ku area 30 B . Mwawakumbukira awa?? Praise team member Eliteck Munthali Inde n...
28/08/2026

Khaaaaaaa another birthday lero
Kuchokera ku area 30 B . Mwawakumbukira awa?? Praise team member Eliteck Munthali
Inde ndiwomewo Inu anabadwa lero tiyeni tiwapatse ma like Awo osaiwala comment🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳

Ineyo nde ndisanamale Fanta ndinamwa kalekale koma anthu awiri awawa andipangisa k*t Saturday ndimweso Fanta ? Ndiku are...
27/08/2026

Ineyo nde ndisanamale Fanta ndinamwa kalekale koma anthu awiri awawa andipangisa k*t Saturday ndimweso Fanta ? Ndiku area 43 kudalitsa komaso perekani perekani

Ndikakhala ine admin wanu zovala ndasankha kale plus ndalama zochitira perekani perekani
Nanga Inu bwaaa??

Letciah and Timothy 🥳🥳🥳🥳🥳

Inu ndikuseli kwamawatu ifeyo nde tili ready Nde mtakufusani Saturday mudzidzatani?? Ndikakhala ine admin wanu nde zoval...
27/08/2026

Inu ndikuseli kwamawatu ifeyo nde tili ready
Nde mtakufusani Saturday mudzidzatani??
Ndikakhala ine admin wanu nde zovala ndasankha kale tikachitire umboni bas it's Gersom Yasin vs Tiwonge Chisamba

Eshiiii tingoti Mr and Mrs Yasin Inu🥳🥳🥳🥳🥳🥳

25/08/2026

Uthenga ochekera ku Sunday school

Sunday yikubwerayi ana akhale akudztsekera Sunday school tiyeni makolo tizatumize anawo nthawi yabwino

Lero ndi birthday ya Sister Chipiliro Suwadi Inu aja amayimba praise team aja Eya ndiomwewo ndithu Anabadwa lero
25/08/2026

Lero ndi birthday ya Sister Chipiliro Suwadi
Inu aja amayimba praise team aja
Eya ndiomwewo ndithu
Anabadwa lero

Lero ndi birthday ya Panashe Kamandani  tiyeni tisangalale naye uyuPaja ndi mmodzi mwama admin a page ino nde paja ndi p...
25/08/2026

Lero ndi birthday ya Panashe Kamandani tiyeni tisangalale naye uyu

Paja ndi mmodzi mwama admin a page ino nde paja ndi photographer 🥳🥳🥳🥳🥳

23/08/2026

Ma Birthday

1. Mr Kamanga Anabadwa pa 22 August

2. Faith William Anabadwa pa 22 August

3. Tawina Kamtwanje anayimira First born wakwawo Anabadwa August

4. Favor Bonga Anabadwa pa 22 August

5 Mrs Kalinde nawo Anabadwa pa 21 August

Happy birthday

Address

Police Headquarters
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Police Headquarters CCAP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share