19/04/2025
Masana ano monga mwa program tikupitila ndi mapemphero a kukumbuchila imfa ndi kuuka kwa kwa Ambuye Yesu. Tsatilani program kuti mutsatsalile. mwambo onse uli live pa tsamba la face book kapena kupanga join pa tsamba la whatsapp ya Msambachikho CCAP family