Seventh day Adventist-SIX MILES District

Seventh day Adventist-SIX MILES District Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Seventh day Adventist-SIX MILES District, Seventh Day Adventist Church, Lilongwe.

Six Miles District, is a demarcation for Seventh-day Adventist Church found in Central Malawi Conference with the Aim of Preaching the Gospel untill the return of Jesus Christ

08/08/2026

SABBATH SCHOOL PROGRAM

Mulungu alemekezeke chifukwa cha atumiki awa amene Mulungu wawagwiritsa ntchito mu msonkhano wa Misasa Chaka Chino. Ma u...
05/08/2026

Mulungu alemekezeke chifukwa cha atumiki awa amene Mulungu wawagwiritsa ntchito mu msonkhano wa Misasa Chaka Chino. Ma uthenga olamitsa, odzudzula, otsitsimutsa ndi kukonzaso. Kupyolera mwa awa Mulungu watiyankhula.

Lasabata Masana azimayi anamalizitsa Zonse. Izi ndi zina mwa zinthuzi zomwe zinatengedwa mu program ya Azimayi pa Mutu o...
04/08/2026

Lasabata Masana azimayi anamalizitsa Zonse. Izi ndi zina mwa zinthuzi zomwe zinatengedwa mu program ya Azimayi pa Mutu oti "Ndidzatuma Yani?".

Uwu ndi usiku omaliza mkati mwa msonkhano wa misasa m'chaka cha 2026. Nyimbo zinavumba komanso ulaliki unalalikidwa.
04/08/2026

Uwu ndi usiku omaliza mkati mwa msonkhano wa misasa m'chaka cha 2026. Nyimbo zinavumba komanso ulaliki unalalikidwa.

Nthambi ya Ana mu chigawo cha Six miles analiso ndi Misasa yawo ndipo lasabata anatiwonetsa zomwe Akhala akuchita. Atiku...
02/08/2026

Nthambi ya Ana mu chigawo cha Six miles analiso ndi Misasa yawo ndipo lasabata anatiwonetsa zomwe Akhala akuchita. Atikumbutsa kumanga nyumba yathu pa thanthwe kuti ingakhale mphepo itabwera tisasunthike

Miracle Makele, this Sabbath's young preacher amaze the congregation with his preaching. Indeed God is still working in ...
01/08/2026

Miracle Makele, this Sabbath's young preacher amaze the congregation with his preaching. Indeed God is still working in young people. If you didn't come, you have missed a lot.

01/08/2026

2026 CHIWENGA CAMP MEETIMG

Mwadzuka bwanji? Mwakapemphera kuti, ife tili Ku Misasa. Inali sabata lopambana kwambiri.
01/08/2026

Mwadzuka bwanji? Mwakapemphera kuti, ife tili Ku Misasa. Inali sabata lopambana kwambiri.

31/07/2026

2026 CHIWENGA CAMP MEETING

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Seventh day Adventist-SIX MILES District posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share