MMS

MMS Every step taken for His sake brings you closer to Jannah.” πŸŒ·βœ…

MMS-MALAWI MUSLIM MOTIVATE SPEECHβ™₯️
Your relationship with Allah is only as strong as your relationship with His creation/people.β€œKeep walking towards Allah, even with small steps.

17/07/2026

Who is Allah

17/07/2026

Assalamu alaikum

help me to mention new boy Muslim name

16/07/2026

Iwe ngati unabadwira banja la chisilamu koma usazitenge ngati wapambana kupambana kumabwera ndikupemphera moyenera

16/07/2026

Tchalani maswahabah awiri omwe adakwatira mwana wa mtumiki s w s

16/07/2026

Kodi ndi mtumiki uti yemwe amakambidwa limodzi ndi Maui ake

16/07/2026

Pakati pa izi zitatu... 😊

❀️ Chikondi - Ndi chomwe chimapangitsa moyo kukhala ndi tanthauzo
πŸ‘ Ndalama - Zimathandiza koma sizikhala ndi inu nthawi zonse
πŸ™ Chisamaliro- Ndi chikondi chomwe chimachitika, osati kungonenedwa

Kwa ine, ndisankha πŸ™ Chisamaliro.
Chifukwa chisamaliro chili ndi zonse ziwiri mkati mwake. Munthu akakusamalira, amakukondanso ndipo amafuna kuwona uli bwino ndi ndalama zako.

15/07/2026

Let's do it and get paradise

γ‚š

15/07/2026

Alhamdulillah for everything weather good πŸ˜‡ or bad πŸ˜₯

15/07/2026

I'm proud to be Muslim and you 😭😭

15/07/2026

This message for believers

Address

Nselema

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MMS posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share