Chinkhuti CCAP Church - Nkhoma Synod

Chinkhuti CCAP Church - Nkhoma Synod Shine on in Jesus Christ

Inuyo mupita kuti Sunday li?Ma ticket a raffle draw alipo kuti inuyo mugule mukhalebe ndi mwayi owina Fertilizer
15/12/2025

Inuyo mupita kuti Sunday li?
Ma ticket a raffle draw alipo kuti inuyo mugule mukhalebe ndi mwayi owina Fertilizer

10/10/2025

CCAP Nkhoma Synod yasankha adindo atsopano pa msonkhano wake omwe unachitikira ku Chongoni m'boma la Dedza pa 9 0ctober.

M'busa Absalom Nyasulu ndiye mkulu wa Synod( Moderator).

M'busa Hamilton Yasin Gama ndi wachiwiri kwa mkulu wa Synod( Vice Moderator).

M'busa Kuthyola wasankhidwa kukhala Mlembi wa Synod ndipo wachiwiri wake ndi M'busa Richard Tamale.

M'busa Richard Tamale asakhidwa pa udindo woona za Malamulo.

M'busa Brian Kamwendo wasankhidwa kukhala Mlembi wa Zonse (GS).

M'busa Kachipanda akupitilira kukhala Wachiwiri kwa Mlembi wa Zonse.

Maudindo awa akhala akuyendetsa Synod kwa zaka ziwiri zikubwerazi pamene GS akhala pa udindowu kwa zaka Zisanu nchimodzi (6).

ndinu oyitanidwa
09/10/2025

ndinu oyitanidwa

He Has Risen
20/04/2025

He Has Risen

You're all Invited
14/04/2025

You're all Invited

14/03/2025
26/01/2025
26/01/2025

Big shout out to our newest top fan! Trìnity Masiye

Make it possible to be attending
26/01/2025

Make it possible to be attending

01/01/2025

Big shout out to our newest top fan! Dorathy Maere

Tikudziwa kuti inu simufuna zabwino zikupiteni ayi. Mawa tili limodzi, Ambuye akudalitseni kwambiri.Tracks1. Asamala2. H...
21/12/2024

Tikudziwa kuti inu simufuna zabwino zikupiteni ayi. Mawa tili limodzi, Ambuye akudalitseni kwambiri.

Tracks
1. Asamala
2. Holy
3. I surrender all
4. Kaone mkhola
5. Mwayenera Yesu
6. Permanent
7. Tamani Ambuye
8. Yamba wathanga
9. Zikomo

Address

Lumbadzi

Opening Hours

06:00 - 17:00

Telephone

+2651700702

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chinkhuti CCAP Church - Nkhoma Synod posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share