Mkochera Ccap Youth

Mkochera Ccap Youth Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mkochera Ccap Youth, Religious organisation, Lilongwe.

24/08/2026

2026 WOMEN'S GUILD ANNUAL CONFERENCE AT CHITIMBE CCAP
FINAL DAY

23/08/2026
23/08/2026

ZOCHITIKA ZA DZULO

Msonkhano wa Amayi 2026 Annual Conference mu Presbytery ya Likuni wapachaka wayamba lero lachinayi ndipo ukutha Lamulung...
20/08/2026

Msonkhano wa Amayi 2026 Annual Conference mu Presbytery ya Likuni wapachaka wayamba lero lachinayi ndipo ukutha Lamulungu ku mpingo wa Chitimbe Ccap .

Ndipo umu ndimomwe Amayi athu atchenele m'masiku amenewa.
See you there!!!

19/08/2026

ULALIKI WA REV KATSALA WAKE "CHIKHULUPILIRO"

17/08/2026



Zomwe zidalipo sabata yangothayi !!!

Bungwe loyang'anira mayeso m'dziko muno la Malawi National Examinations Board (MANEB), mogwirizana  ndi unduna oona za m...
16/08/2026

Bungwe loyang'anira mayeso m'dziko muno la Malawi National Examinations Board (MANEB), mogwirizana ndi unduna oona za maphunziro latulutsa zotsatira za mayeso a Primary School Leaving Certificate of Education (PSLCE) ndi Junior Certificate of Education (JCE).

Ophunzira okwana 245,048 ndiomwe analemba mayeso a PSLCE ndipo ophunzira okwana 198,903 ndi omwe akhoza kuyimilira 81.17 pa handede iliyonse, anyamata akhonza okwana 81.17% pomwe atsikana akhonza okwana 76.94%, pa ophunzira omwe ali ndi ulumali 2,726 ndi omwe analemba mayeso omwe akhonza ndi 1,949 kuyimilira 71.50%

Bungweli lati ophunzira okwana 154,880 ndi omwe analemba mayeso a JCE ndipo 125,777 ndiomwe akhonza kuyimilira 81.2 pa handede iiyonse ndipo anyamata akhonza okwana 84.04 pa handede iliyonse, pomwe atsikana akhonza 78.49 pa handede ili yonse, ku ophunzira amene ali ndi ulumali analemba okwana 978 okwana 806 ndi omwe akhonza kuyimilila 82.41 pa handede iliyonse.

Malo omwe amalembetsa mayeso atha kupeza zotsatilazi kudzela pa e-Registration Portal, pomwe ophunzira kapena makolo atha kupeza zotsatilazi kudzera pa MANEB Examination Results Portal pogwilitsa ntchito nambala ya mayeso yoyenelera komanso tsiku lobadwa.

Wolemba: Mkochera Ccap Youth Media

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mkochera Ccap Youth posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share