Msundwe Assemblies Church

Msundwe Assemblies Church We exist to please the Most High King Jesus Christ as we await for His second coming!

01/09/2022

Tiri ndi Group Paper Sunday pa 4 September 2022 lomwe ndi Sunday likubwerari. Cholinga ndikumanga church cha pamwamba chandalama zosachepera 50 million kwacha. Target patsikuli ndi 10million kwacha... Tidzakhala ndi anthu ochokera ku Malomo Assemblies of God in Ntchisi, kasungu Assemblies of God and others from Dowa. Kudzabweraso Patricia Kaliat, Jinny Sendeza and MPs... come and give to the Lord!

05/07/2022

Tiri mmasiku osautsa! Masiku ammene anthu tikufuna uthenga osisitana osati olamitsa! Masiku amene otsutsana ndi uchimo ndiye kape ochita tchimo ndiye dolo. Odala iwo amene ayimebe ndi Yesu Khristu kufikira kudza kwake!

19/06/2022

Bishop Dr. Andrew Dube Officially Launching the Construction of Msundwe Assemblies of God Mega Church.....

19/06/2022

Official Launching of Msundwe Assemblies of God Mega Church Construction... by Bishop Dr. Andrew Dube, President of Malawi Assemblies of God.

Msundwe Assemblies of God Praise Team
19/06/2022

Msundwe Assemblies of God Praise Team

Come one! Come all!
24/05/2022

Come one! Come all!

18/11/2021

Sunday ikubwerayi ndi Men's day......

29/09/2021

MEMBERS
I would like to inform you that am failing to make the group open to everyone so that we can all be able to view messages sent by every member. If there is someone who has got a tip on how to make it open to every member plz hit my inbox.

06/05/2021

Ndi oyimba nyimbo za uzimu utiyo yemwe mumatsitsimuka kwambiri ndi nyimbo zake? Ine Benjamin Dube eeeeeishhh nyimbo zake zimandikankhira kwakuyaaa

22/04/2021

Koma ikudza nthaw ndipo tsopano ilipo imene olambira owona adzalambira Atate mu mzimu ndi nchoonadi. Hallelujah!

03/04/2021

Only the righteous shall enter heaven, there is neither corruption nor bribery! LETS LIVE HOLY LIFE!!!

30/03/2021

Ndi nyimbo iti ya m'buku la Chitsitsimutso yomwe imakusunthani kwambiri? Ine number 2, ndiyimba ndichimwemwe lero kale ndinalephera wandichotsera Yesu tchimo ooh Hallelujah!

Address

Msundwe Trading Center Alongside Mchinji Road
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Msundwe Assemblies Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share