Gologota SDA Church

Gologota SDA Church Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Gologota SDA Church, Religious organisation, Lilongwe.

11 Days More
26/08/2026

11 Days More

22 August, mpingo wa Gologota umatsekera msonkhano wa chitsitsimutso omwe wakhala ukchitika kwa masabata awiri. Anthu 20...
25/08/2026

22 August, mpingo wa Gologota umatsekera msonkhano wa chitsitsimutso omwe wakhala ukchitika kwa masabata awiri. Anthu 20 ndiwo asankha Yesu Khristu kudzera mu ubatizo.

Msonkhanowu umatsogozedwa ndi atsikana a Gologota Young Dorcas pamutu wakuti "Yesu akubwera konzani mtima wanu'. Mlaliki Susan Chikandira nde wakhala ukupereka Uthenga Wabwino mmasiku onse 14.

Kawale Young Dorcas ndi Area 38 Young Dorcas anali alendo patsikuli.

13 Days to go
24/08/2026

13 Days to go

14 Days to go 2026 Area 23 District SDA Church Camp Meeting
23/08/2026

14 Days to go
2026 Area 23 District SDA Church Camp Meeting

22/08/2026

SABBATH WORSHIP | AFTERNOON PROGRAM

22/08/2026

SABBATH SCHOOL HIGHLIGHTS

SABATH SCHOOL PICTORIAL
22/08/2026

SABATH SCHOOL PICTORIAL

Mukhale ndi sabata lopambana pamene tikutsekera msonkhano wa chitsitsimutso.
22/08/2026

Mukhale ndi sabata lopambana pamene tikutsekera msonkhano wa chitsitsimutso.

20/08/2026

DAY 12 | MSONKHANO WACHITSITSIMUTSO

DAY  #12 TOPIC: TCHIMO LOSAKHULULUKIDWA LIPWENI NSANGA.
20/08/2026

DAY #12
TOPIC: TCHIMO LOSAKHULULUKIDWA LIPWENI NSANGA.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gologota SDA Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share