Katate CCAP Church

Katate CCAP Church Teaching and preaching the word of our Lord Jesus Christ

25/08/2026

Achinyamata anzanga Kodi mwapakira kale? Misonkhano yatipanikiza 🥳🥳🥳

23/08/2026

welcome

Mawa pa 23.08.26 ndi tsiku la Worship Sunday komanso Prayer and Fasting kuthokoza Mulungu chifukwa cha msonkhano wabwino...
22/08/2026

Mawa pa 23.08.26 ndi tsiku la Worship Sunday komanso Prayer and Fasting kuthokoza Mulungu chifukwa cha msonkhano wabwino ndi wopambana womwe tinali nawo sabata lomwe langothali. Tiyeni abwenzi tisajombe ayi. Service idzakhalapo imodzi ndipo ikudzayamba nthawi ya 8 o'clock mpaka 4 o'clock madzulo. Tiyeni tikumane kumeneku. 🥳🥳

21/08/2026

Abwenzi!
Panali ena ake anapempha nyimbo za msonkhano za Katate CCAP, mukaona message iyi tilankhuleni ku inbox kuti tikutumizireni. Pangani hie pa 0884645736. Zikomo.

18/08/2026

Address

Likuni
Lilongwe

Telephone

+265999472553

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Katate CCAP Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share