St. Dominic Savio youth choir

St. Dominic Savio youth choir Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from St. Dominic Savio youth choir, Religious organisation, St. Lazarus Church, Mdeka, Blantyre.

Good Morning St. Dominic Savio youth choir
11/08/2026

Good Morning
St. Dominic Savio youth choir

Chiimba chili m'mimba. Timadya Kaye kuti tiimbe mwamphavuSt. Dominic Savio youth choir
10/08/2026

Chiimba chili m'mimba.
Timadya Kaye kuti tiimbe mwamphavu

St. Dominic Savio youth choir

happy Sunday, πŸ’₯πŸ’₯
09/08/2026

happy Sunday, πŸ’₯πŸ’₯

kumwamba ndithu kukoma awusako anthukomweko asangalala Poona Mulungu. πŸ’” Ause ndi Mtendere Brian BandaπŸ’”πŸ’”
08/08/2026

kumwamba ndithu kukoma awusako anthu
komweko asangalala Poona Mulungu.
πŸ’” Ause ndi Mtendere Brian BandaπŸ’”πŸ’”

Munda wakula antchito aperewera...  Awa ndi achinyamata a St. Lazarus chapel  πŸ’’ tiyeni tigwirane nawo manja pofalisa uth...
02/08/2026

Munda wakula antchito aperewera...

Awa ndi achinyamata a St. Lazarus chapel πŸ’’ tiyeni tigwirane nawo manja pofalisa uthenga wa Ambuye
Mzina la Atate ndi Lamwana ndi la Mzimu oyera.... Amen

Happy birthday mnyamata wa tenor πŸŽ‰πŸŽˆ enjoy your day
02/08/2026

Happy birthday mnyamata wa tenor πŸŽ‰πŸŽˆ enjoy your day

21/07/2026

St. Dominic Savio Choir,
Tiyeni tikaimbire Ambuye
🎹🎸🎺🎷🎀🎀🎧🎧

Ife tapemphera bwino, inu mwapemphera bwanji komwe muliko?? St. Dominic Savio youth followers
12/07/2026

Ife tapemphera bwino,
inu mwapemphera bwanji komwe muliko??
St. Dominic Savio youth followers

11/07/2026

(Ndi zikomo) by fr. Jean Marrie all the way from DRC.

St. Dominic Savio youth choir

wachinyamata wa mzeru amayamba chitukuko cha moyo wake pang'ono pang'ono.mwatandala uliSt. Dominic Savio youth choir
10/07/2026

wachinyamata wa mzeru amayamba chitukuko cha moyo wake pang'ono pang'ono.

mwatandala uli
St. Dominic Savio youth choir

Address

St. Lazarus Church, Mdeka
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when St. Dominic Savio youth choir posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share