Citizen zion city church

Citizen zion city church Prayers & healing sickness

20/02/2024
21/03/2023

*MISONKHANO YOYIKIDWA MU ZAMBIA CAKA CHA 2023.*

*YA P***A*

1. *20/04/2023* - KALONGO BRANCH MU BOMA YA PETAUKE.

2. *20/07/2023* - PUNZA BRANCH MU BOMA YA PETAUKE.

3. *17/08/2023* - UZAKHALA KU DERA YAKU MIGODI ( COPPERBELT) NDIPO BRANCH TIZAUZIDWA MSOGOLO.

4. *12/10/2023* - LUNENE BRANCH MU BOMA LA PETAUKE.

*YA AZIMAI*

1. *07/09/2023* - NYALUKOMBA BRANCH MU BOMA LA PETAUKE.

2. *21/09/2023* - KANYAMA BRANCH M'ZINDA WA LUSAKA.

*YA MAKHWAYA*

1. *08/06/2023* - CHAWAMA BRANCH MU M'ZINDA WA LUSAKA.

2. *03/08/2023* - KACHANGA BRANCH MU BOMA YA PETAUKE.

*_MULUNGU AKUDALISENI!!*_

03/03/2023

Pa zion

02/03/2023

Yeremia 9 : 26
apena tiyambira apa mau a yeremiya ameneyu 25Taonani, masiku alikudza, ati Yehova, kuti ndidzalanga onse odulidwa m'kusadulidwa kwao; 26Aigupto, ndi Yuda, ndi Edomu, ndi ana a Amoni, ndi a Moabu, ndi onse ometa m'mphepete mwa tsitsi lao, okhala m'cipululu; pakuti amitundu onse ali osadulidwa, ndi nyumba ya Israyeli iri Yosadulidwa m'mtima Amen mwaswerabwanji abale nonse mwa Ambuye wathu Yesu kristo.ine mwanu Mulembi Yesaya ndachomabwino kuno ku MoΓ§ambique

02/03/2023

Announcement from Lusaka ZambiaπŸ‡ΏπŸ‡²
Good evening all people this group good news on Saturday 4/03/23 general meeting kanyama branch time 08: hr

02/03/2023

Buku Lopatulika 1992 Yeremiya 9:26 Aigupto, ndi Yuda, ndi Edomu, ndi ana a Amoni, ndi a Moabu, ndi onse ometa m'mphepete mwa tsitsi lao, okhala m'cipululu; pakuti amitundu onse ali osadulidwa, ndi nyumba ya Israyeli iri Yosadulidwa m'mtima.

28/02/2023

*πŸ“–πŸ“–OPEN HEAVENS DAILY DEVOTIONAL GUIDE.*

*DATE: TUESDAY 28TH FEBRUARY, 2023*

*THEME: THE MOST HIGH*

MEMORISE:
β€œFor the LORD most high is terrible; he is a great King over all the earth.” – (Psalm 47:2)

READ: Psalm 47:1-7 (KJV)

1 O clap your hands, all ye people; shout unto God with the voice of triumph.

2 For the LORD most high is terrible; he is a great King over all the earth.

3 He shall subdue the people under us, and the nations under our feet.

4 He shall choose our inheritance for us, the excellency of Jacob whom he loved. Selah.

5 God is gone up with a shout, the LORD with the sound of a trumpet.

6 Sing praises to God, sing praises: sing praises unto our King, sing praises.

7 For God is the King of all the earth: sing ye praises with understanding.

MESSAGE:
There are many great leaders in this world. However, there is Someone called the Most High, the Almighty (Psalm 91:1). He is higher than the highest (Ecclesiastes 5:8). Isaiah 66:1 says heaven is His throne and the earth is His footstool.

According to Revelation 19:16, He is the King of kings. Put in modern terms, He is the President of all the presidents in the world.

The Most High God rules in the affairs of men (Daniel 4:25). In Daniel 4:34-35, the king of the country considered as the superpower in the world at that time confessed that the dominion of the Most High is forever.

Thus, once in a while, when one earthly leader or the other is beginning to feel big and in control, God teaches the fellow a lesson and shows the whole world that He is still in control. God demonstrated through the Coronavirus pandemic that despite the sophistication of the leaders of the world, they are powerless without Him and so they must surrender to His Lordship.

Proverbs 21:1 says He is the one who controls the heart of kings like rivers of water. When an earthly king is beginning to prove stubborn and refuses to bow to His Lordship, He can deal with the fellow in one of two ways. The first is

24/02/2023

Mlaliki 3vs1

Ziri zofise ziri ndi nyengo yace, Mulungu ndi kuziika zonse

1Kanthu kali konse kali ndi nthawi yace ndi cofuna ciri conse ca pansi pa thambo ciri ndi mphindi yace; 2mphindi yakubadwa ndi mphindi yakumwalira; mphindi yakubzyala ndi mphindi yakuzula zobzyalazo; 3mphindi yakupha ndi mphindi yakuciza; mphindi yakupasula ndi mphindi yakumanga; 4mphindi yakugwa misozi ndi mphindi yakuseka; mphindi yakulira ndi mphindi yakubvina; 5mphindi yakutaya miyala ndi mphindi yakukundika miyala; mphindi yakufungatirana ndi mphindi yakuleka kufungatirana;

19/02/2023

π™ΌπšŠπšπšŠπš•πš’πšœπš˜ πšŒπš‘πšžπš›πšŒπš πšŒπš‘πš˜πš’πš›
π™Όπš πšŠπš—πš“πšŠπš πšŠπš—πšπš‘πšž πš‘πšŽπšŠπšπššπšžπšŠπš•πšπšŽπš›.

19/02/2023

π™ΆπšŠπš•πšŠπš–πšžπš”πšŠπš—πš’ πšŒπš‘πšžπš›πšŒπš‘ πšŒπš‘πš˜πš’πš›
πš–πš πšŠπš—πš“πšŠπš πšŠπš—πšπš‘πšž πš‘πšŽπšŠπšπššπšžπšŠπš•πšπšŽπš›.

18/02/2023

Chakudya chathu m'mawa uno

Masalimo 23 vs 1

Amwai amene Yehova akhala Mbusa wao

Salimo la Davide,
1Yehova ndiye mbusa wanga; sindidzasowa.
2Andigonetsa ku busa lamsipu:
Anditsogolera ku madzi ndikha.
3Atsitsimutsa moyo wanga;
Anditsogolera m'mabande a cilungamo, cifukwa ca dzina lace.
4Inde, ndingakhale ndiyenda m'cigwa ca mthunzi wa Imfa,
Sindidzaopa coipa; pakuti Inu muli ndi ine:
Cibonga canu ndi ndodo yanu, izi zindisangalatsa ine,
5Mundiyalikira gome pamaso panga m'kuona kwa adani anga:
Mwandidzoza mutu wanga mafuta; cikho canga cisefuka.
6Inde ukoma ndi cifundo zidzanditsata masiku onse a moyo wanga:
Ndipo ndidzakhala m'nyumba ya Yehova masiku onse.

Ambuye akudalitseni nonse amene pamabvuto pamtendere yehova adzakhala m'busa wanu,ndipo mudzadalira mulungu
Amen

Address

Petauke

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Citizen zion city church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share