New Generation Ministry

New Generation Ministry Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from New Generation Ministry, Religious organisation, 13/11 Street, Randburg.

This is a religious group aimed at leading people into savation and also we to sort out all problems that people may experience through Christ jesus the son of living God

08/03/2021
01/11/2020

Palibe chida chomwe chizasulidwira inu ndpo chizapambane ingokhulupiliran mulungu kosalekeza

24/09/2020

Palibenso nsembe ina yomwe mulungu azaipereke yoposera yomwe anaipereka yotipatsa mwana wake yesu nkhristu kuzafela inu ndi ine

13/09/2020

Musamazione ngat ndnu munthu osiyidwa kapena osalidwa pamanso pamulungu dzindkiran k*ti mulungu amagwritsa ntchto zinthu zonyozeka k*t akachititse manyazi anthu ooneka ngat ozindikira.anthu amene akukunyozan lero azakudabwan mulungu atasintha nyengo zanu chifukwa palibe uyo ndi mmodzi amene adziwa zatsogolo lanu

12/09/2020

Palibe wna ali ndk*thekera kopulumutsa moyo wako kupatula mulungu tulan nkhawa zanu kwamulungu popeza iye samagona tulo amamvesera nthawi zonse

08/09/2020

Jesus said am the way the truth and the life no one come into my father except through me,,,so I request everybody elsewhere you are that you are not late this is your time to stop all what you are doing and start doing things that will pleasing God and he is ready to receive you as his son or daughter

08/09/2020

Mulungu yemwe anatulutsa ana aisrael mu ukapolo ndiyemweyo amene akuyenera kukupulumutsan inu munyengo zowawitsa zomwe mukudutsamo.

Address

13/11 Street
Randburg

Telephone

+265995412374

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when New Generation Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share