Friends of hope

Friends of hope Teaching and leaning the word of Lord

18/04/2022

Ambuye akalemekezeke Ku nthawi ino ya m'mawa wa tsiku lolemba pa 18April 2022,ndikuziwa ena mukuzifunsa Kuti mwapezeka bwanji tsiku la lero ,ziwani kuti kupezeka kwanu Kwa tsiku la lero Ambuye ali ndi cholinga chomwe akufuna Kuti mukakwanilitse,abale wathu wena tikunena pano atsikila kuli chete Koma inu ndi ine tili ndi moyo tiyeni timutamande Ambuye ponena Kuti "Dzikomo Ambuye chifukwa cha moyo omwe mwandipasa tsiku la lero mukalemekezeke ndi kukatamandika masiku onse a moyo wanga" Ambuye akudaliseni nonse kuyambila tsopano kudikila nthawi za nthawi.

Amen

May God be blessed amen
19/03/2022

May God be blessed amen

14/12/2021

God is good all the time

16/04/2021

Good morning Friends of hope members?

Do you know that God have mercy on us?

Let's thank him for the life we have today

Just type THANK YOU GOD FOR THE LIFE I HAVE TODAY.

God bless you all.

19/02/2021

Ambuye atisogolere usiku uno kufikila tikaonenso ulemelero wa mphamvu yake kudzera ku dzuwa ntsiku lina lili mkudza, Ambuye akudaliseni ndi kukutetezelani nonse

10/02/2021

Ambuye ndi wadongosolo ndipo palibe amene angamulamule,onani lero inu ndi ine tadzukanso ndi moyo ,cholekela kumuyamika ndi chani abale wanga?

Ambuye mukalemekezeke chifukwa cha moyo wa mphamvu omwe mwandipatsa lero,onani ndinali ngati munthu wakufa koma mwandidzutsa kundionetsa ulemelero wanu wa mphamvu ya dzuwa Baba ndikuti zikomo, mukalemekezeke kuyambira pano kufikila ku chimalizilo cha nthawi mukandiongolele ndinu Mulungu wanga,Baba mwapadela ndikukupemphani kuti mukawayendere onse omwe akumva zowawa mkati mwa miyoyo yawo ndi mukatenge dzanja lanu la machilitso ndi mukawakhuze mkuwachotsela nthenda zawo, mukalemekezeke ndi kutamandika nthawi zonse , Amen.

13/01/2021

Mwadzuka bwanji nonse tsiku labwino kwambiri lomwe Ambuye atipasa tiyamike kumwamba kamba ka tsiku longa ili lomwe ena sadalione koma inu ndi ine tili moyo lero chifukwa cha mphamvu yomwe Atate Wathu aiuzila mpheya mwa ife,popanda kutiuzila mpheya tsiku la lero sitikadaliona,zikomo mbuye wanga mukalemekezeke ndinu kuyambila tsopano kupita ntsogolo,Amen.

02/01/2021
01/01/2021

Happy new year to you all friends of hope,I hope you will enjoy your new year and fulfil all what you have failed to achieve for the past years,ask God and ask with hope because God never fail,Am wishing you all a glorious day as well as a year (2021) of deliverance. God be with you

25/12/2020

Ambuye wa matamando akalemekezeke, pamene watkbsdwila tsiku lero yiyeni tikabadwe naye limodzi ndipo tikayende naye kwina kuli konse, zowawa zomwe adaziona tikazionele limodzi, Mulungu akudaliseni nonse popanga chisankho chobadwa,kuzunzika,kumenyedwa ,kuphedwa,kupachikidwa pa ntanda ndi kuuka naye kumka ku mpando wa chifumu kumwamba, Mulungu akudaliseni nonse mukhala ndi chitsangalaro cha Christmas chopambana

Address

Nobulerol
Port Elizabeth

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Friends of hope posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share