CCAP Joburg City Congregation

CCAP Joburg City Congregation Church services and testimonies, morning and night devotions, inspirations etc

12/08/2026

Munyengo zonse ,nowadays kaya zachisangalalo osasiya kumpepedza Mulungu

11/08/2026

Osamachuluka nzeru ndi chinthu chopatsidwa mwaulere ndikuyambaso kunyoza kapena kuderera okupatsayo. Ngozi osamaiyamba dala.

09/08/2026

SUNDAY LIVE SERVICE

07/08/2026

MAU WODZUKILA MORNING WATCH

Ndipo Davide anati, kodi atsalako wina wa nyumba ya Sauli, kuti ndimchitire chifundo chifukwa cha Jonatani?

2 SAMUELI 9:1📖🛏️
Moyo uno zikufunika kumakhala bwino ndi anthu kupangira pamawa ndi zomwe zimadzathandiza ana athu ife kulibe, Davide akukumbukira zomwe Jonathan anamuchitira tiphunzire kulemekeza anthu kuopa mawa
Mukhale ndi tsiku lopambana nonse

04/08/2026

Nkhomaliro ya lero

The preacher and the Message.
03/08/2026

The preacher and the Message.

02/08/2026

Isn't this beautiful? Hilbrow Church Choir

02/08/2026

Are you not coming today? Madodona ayambatu.

30/07/2026

Mu chichristu tukumana nama unonono

30/07/2026

Waking up to this Gospel? It's not coincidence, it's God's Will and Blessings to you this morning. Be blessed as you prepare for work, business and other ventures.

Address

66 End Street
Johannesburg

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CCAP Joburg City Congregation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to CCAP Joburg City Congregation:

Shortcuts

Share