Favoured Ambassadors International Ministries

Favoured Ambassadors International Ministries BRINGING SOULS TO GOD

YESAYA 60:2222Wamng'ono adzasanduka cikwi, ndi wocepa adzasanduka mtundu wamphamvu; Ine Yehova ndidzafulumiza ici m'ntha...
12/06/2025

YESAYA 60:22

22Wamng'ono adzasanduka cikwi, ndi wocepa adzasanduka mtundu wamphamvu; Ine Yehova ndidzafulumiza ici m'nthawi yace.

OKONDEDWA IKAKHALA NTHAWI YA KUMWAMBA NGAKHALE ZITACHEDWA KOMA ZIKAFIKA SUPANGA REGRET. VUTO PHUMA, CHANGU INUYO, KAYA MUKUTHAMANGILA KUTI?

*AMBUYE ATITHANDIZE KUDIKILA PA IYE*

05/03/2024

Kumwamba kukakuendera, anthu adzikambirana

05/03/2024

Kumaziyeza okondedwa

19/02/2024
05/01/2024

THANKS FOR YOUR TIME SONS AND DAUGHTER IN THE LORD

Popanda masomphenya anthu amavutika . Masomphenya ndi gwero la ulendo ulionse       ndipo popanda masomphenya timasocher...
11/12/2023

Popanda masomphenya anthu amavutika . Masomphenya ndi gwero la ulendo ulionse ndipo popanda masomphenya timasochera kapena kubwerera chifukwa zobwemza mu ulenduwu ndi ZOCHULUKA koma ukaendabe pa masomphenya susochera kapena kubwerera koma kupitabe chitsogolo ambuye atithandize kuyendabe mdzina la christu Yesu

Don't miss it
05/10/2022

Don't miss it

Address

Jo'burg Mall
Johannesburg

Telephone

+27834922342

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Favoured Ambassadors International Ministries posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Favoured Ambassadors International Ministries:

Share