13/09/2025
2 Akorinto : 11 :13-14
13. Pak*ti anthu oterewa ndi atumwi onama, antchito achinyengo, odzizimbayitsa ngati atumwi a Khristu.14. Sizododometsa zimenezi, pak*ti Satana mwini amadzizimbayitsa kuoneka ngati mngelo wowunikira anthu.
*Hallelujah ππ½ππ½ππ½ππ½!!Tiri masiku otsiliza amene panopo mwa anthu 100 ndi anthu mwina awiri or atatu amene akupempha mu mchoonadi,masiku ano ambiriwa ndi satana weni weni ndipo or k*t muve uthenga wao zosiyana k*tali tali ndi Baibulo,Kmatu izi ndimphavu a satana kufuna kunyenga ambiri,inu anthu pano kupemphera kwafika pa business,kwafika pa ndale,aliyese akufuna kt mpingo wake udzaze,Indeee Yesu anat tipemphe mwini munda kt atipase antchito ena,Kma Kuno ku Hermanus ma church ali paliponse,and kt muone muona kt church cina anthu 8,mwina 7,mwina 15 akakhala ambiri zedi mwina 30,Izizi zikukwaniritsa malemba kt ndi masiku otsizadi ndithu aliyese akufuna k*tchuka ndi ndalama,Bwanji osapanga mpingo umodzi ngat mukupemphera mu mchoonadi!?? ndipo satana akugwiritsa ntchito azitsogoleri athuwa kukhala ngat opemphera pamene ai ndthu,satana wangosintha kukhala ngat m'ngero,tisamale awawa si azitumiki a Yesu Khristu ai,tiyen once again tipemphe mzimu wa cidziwitso azibale anga ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½ππ½*