15/03/2025
STANDARDS
Jeremiah 17:9-10
[9]“Who can understand the human heart? There is nothing else so deceitful; it is too sick to be healed.
[10]I, the Lord, search human minds and test human hearts. I treat each one according to the way he lives, according to what he does.”
Kazindikililo ka mulungu ndi munthu nkodiyana ndithu ngati pakufuna chiweluzo.
Munthu amaweluza malingana ndi mawonekedwe akunja maka maka ndi zintchito zamunthuyo mmene maso oweluzayo akuwonela. Amene ali oweluza onama munthu samaweluza zenizeni pakuti chimene aweluzila wina naye nchimwe amachita ndipo adzeyeluzidwa ndichimwecho. Chimene chikusonyeza kuti anthu wonsebamangofanana basi zosiyana zomangokhala zochita chita basi.
Mulungu ndiye woweluza weni weni salingati munthu . iye samayang'ana Za ntchito yamunthu, mayendedwe, kapenyedwe,kavalidwe, kakhalidwe, mayankhulidwe. kufuwoka, wa mphamvu, wawulesi, wochilimika, wachikondi, wankhanza wolemela kapena wosauka. Mulungu salabadila sosenzi, koma iye amaweluza malingana ndi mkati mwantima wamunthu. Mntima wa munthu ndi nkhokwe yazambili, munthu atha kuganiza kuti muli chimanga pamene muli mapila kapena ntedza ndeno mulungu amaweluza malingana ndizimene zili mkatimo. Zimenezi munthu sangaziwone.
Munthu wabwino kwa ife kwa mulungu amakhala nunkha dala amene ali nunkha dala kwa ife kwamulungu amakhala bwenzi la panyima pake.
Romans 9:11,13,15-18
[11](11-12) But in order that the choice of one son might be completely the result of God's own purpose, God said to her, “The elder will serve the younger.” He said this before they were born, before they had done anything either good or bad; so God's choice was based on his call, and not on anything they had done.
[13]As the scripture says, “I loved Jacob, but I hated Esau.”
[15]For he said to Moses, “I will have mercy on anyone I wish; I will take pity on anyone I wish.”
[16]So then, everything depends, not on what human beings want or do, but only on God's mercy.
Ndizapiyiliza nkhaniyi.
Send a message to learn more