02/03/2026
Mulungu analenga ku mwamba ndi dziko lapasi, kotero anapatsa mwana wake obadwa ekha, kuti yese Okhulupilira iye asatayike koma akhale nawo moyo wasatha.
Abale, kulebeso kwina tingapite ndi mavuto athu, koma ndi kwa Mulungu ekha basi. HALLELUJAH ๐