Pastor Malemba

Pastor Malemba GATHERING IN CHRIST GLOBAL MINISTRY📖🌍

Revealing JESUS & his finished work on the cross.
(1)

27/08/2026

Phone Yako ili online pa FB nthawi zino?

RECEIVE MADALITSO AKO ANTHAWI INOYO!

MZIKHALA BWINO NDI MUNTHU ALIYENSE ‎AHEBRI 13 VS 2.‎Pitirizani kukondana monga abale. Musayiwale kusamalira alendo, paku...
27/08/2026

MZIKHALA BWINO NDI MUNTHU ALIYENSE

‎AHEBRI 13 VS 2.
‎Pitirizani kukondana monga abale. Musayiwale kusamalira alendo, pakuti pochita zimenezi anthu ena anasamalira angelo amene samawadziwa.
‎Ahebri 13:1-2
‎
‎OKONDEDWA PAMENE KWACHAPA TIYENI TIKHALE ANTHU OKONDA ALIYENSE AMENE TILANKHULE NAYE LERO .
‎
‎PAKUTI SITIDZIWA CHIMENE ALI MUNTHUYO.
‎PAKUTI MKUTHEKA WANYAMULA MDALITSO WATHU.POSATENGERA NDI OWONEKA BWANJI KOMASO TIYENI TIKHALE ANTHU OCHITA MTENDERE NDI ANTHU ONSE AMENE TILANKHULE NAO. TIKUTI POSATENGERA MAONEKEDWE AMUNTHUYO, MAKAMAKA MUNTHU OSAMUDZIWA.
‎
‎OKONDEDWA TAVANIKO UMBONI UWU.👇
‎
‎TSIKULINA LAKE MNYAMATA WINA, AMAPITA KUMAYESO OFUSIRA NTCHITO. NDIYE ALI BUS, MUDAKWERA ENA OMWE SAMAONEKA KUTI NDI ABWANA. NDIYE ABWANAWA ADAPONDA SAPATO YA MNYAMATA UJA MWANGOZI.
‎
‎OKONDEDWA TAVETSERA!
‎
‎MNYAMATA UJA ADAYAMBA KUNYOZA ABWANA AJA, OMWESO ADALI ABWANA ANGA, NDIYE TITATSIKA INE NDIDAWALANDIRA CHIKWAMA ABWANA AJA ULENDO WAKU NTCHITO KWATHU. TSIKU ILI LIDALI LAMAYESO KWA ANTHU UFUNA NTCHITO PACHIPATALA. ABWANA ADANDITUMA KUTI NDIGAWE MAFOMU KWA ONSE ADABWERA KUFUNA NTCHITO.
‎
‎OKONDEDWA TAVETSERANI INUUUU! MNYAMATA UJA ADAPEZEKA PA GULU LIJA, YEKHA ADADZIWIRATU KUTI YALAKWA,
‎
‎PAKUTI ABWANA AJA AMAKONDA KUDUTSA DUTSA NDIKUMANDITUMA MNYAMATA UJA KUTI AZINDIKIRE KUTI AMANYOZA MUNTHU OFUNIKIRA KWAMBIRI.
‎
‎NDIYE IZI ADACHITA ABWANA AJA AKUTI , ELLA UYU ALOWE MUNO MOMALIZIRA NDIFUNA NDIMULANDIRITSE YESU, PAZIJA WANDIPANGA INE MMAWA ZIJA.
‎
‎
‎ALLERUYA NGWAZI ZA YAWEH
‎
‎OKONDEDWA AMBIRI ADATAYA MWAI CHIFUKWA CHAKHALIDWE LOKONDA KUNYOZA, MAKAMAKA KUNYOZA MUNTHU OSAMUDZIWA
‎
‎MATEYU 5 VS 9
‎
‎MOTI PAMENE KWACHAPA TIYENI TIKHALE ANTHU CHITA MTENDERE NDI ANTHU ONSE, PAKUTI MWINA TINGATAYE MWAI WATHU.
‎
‎MUKHALE NDI TSIKU LOPAMBANA PAMENE MUPANGA CHISANKHO CHOKHALA ANTHU AMTENDERE🙏
‎

26/08/2026

Usanagone iweyo ukuwerengawe

MULUNGU AKWANILITSE MASOMPHENYA AKO

‎Munthu atsatile zipangano zonse Koma kuti Timadziwa komwe nkhani ikuchoka ndikumene ikupita Chipangano Chakale nkhumba ...
26/08/2026

‎Munthu atsatile zipangano zonse Koma kuti Timadziwa komwe nkhani ikuchoka ndikumene ikupita Chipangano Chakale nkhumba inali yodetsedwa Chipangano Chatsopano Siyodetsedwaso ai Kudziwa kumene Nkhani ikuchoka ndikumene ikupita. Kumbali ya CHIPULUMUTSO ANTHU ikumativuta kunvetsetsa chifukwa timatsatira chipangano chakale.
‎
‎Chipangano Chakale Tsiku lopembedza Lashisanu ndi Chiwiri Chipangano Chatsopano OKHULUPILILA Akusonkhana Loyamba La Sabata 1Akorinto 16:2 Machitidwe 20:7. Kudziwa kumene Nkhani ikuchoka ndikumene ikupita
‎
‎Chipangano Chakale Amapha nsembe nkhosa ,mbuzi ndi zina. Koma Chipangano Chatsopano nsembe ndi YESU KHRISTU. Sitingapelekeso ngati m'mene amapelekela Chipangano Chakale kudziwa kumene Nkhani ikuchoka ndikumene ikupita.
‎
‎Amene Akutsatila Chipangano Chatsopano ndamene akutsatila Chipangano Chakale popeza Chipangano Chakale ndi Chifanizilo Chatsopano ndiye Chosatha. ZIKOMO 🙏
‎

26/08/2026

WACHITA MPHUMI KUONA POST IYI

pompano pompano Chodabwitsa chichitike pamoyo wako iwe

26/08/2026

Kodi uli online?

Sindikukamba za mawa koma lero kusanade ULANDILE UTHENGA WA NDALAMA

‎Ndinaphunzira kuti anzanga si onse amakhala mpaka kalekale. Ena amabwera kudza "ndiphunzitsa phunziro, ena amabwera kun...
26/08/2026

‎Ndinaphunzira kuti anzanga si onse amakhala mpaka kalekale. Ena amabwera kudza "ndiphunzitsa phunziro, ena amabwera kundithandiza pa nthawi inayake, ndipo ena amachoka. Sindikwiya ndi zimenezo, chifukwa moyo umapitirira. Anthu oyenera adzakhala, ndipo amene ayenera kuchoka adzachoka.🙏
‎
‎
‎Tikuona Yosefe anagulitsidwa ndi azibale ake NDIPO anakakhala kapolo ku dziko la iguputo koma mu zonsezi sizinampangitse MULUNGU kumutaya Josefe ndipo mpaka anakwezedwa KUKHALA MINISTER MU DZIKO IGUPUTO
‎
‎Woyangʼanira ndende uja sankayangʼaniranso china chilichonse chimene chinali mu ulamuliro wa Yosefe, chifukwa Yehova anali ndi Yosefe. Ndipo Yehova anaonetsetsa kuti chilichonse chimene Yosefe ankachita chimuyendere bwino.
‎Genesis 39:23
‎
‎

26/08/2026

Chokhacho chongowona post iyi uli ndi MPHUMI!

UMASULIDWEE PAMENE ULIPO

25/08/2026

kugwira phone Yako panopo sunabetse

MULUNGU AKUTI WAYANKHA MAPEMPHERO AKO AJA đź’Ş

25/08/2026

ma plan ANU mukasanja MUZIONA ANTHU ake owauza ANTHU ena ndi oyipaaa

Address

Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pastor Malemba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Pastor Malemba:

Shortcuts

Share