Zomba Living coner stone international church

Zomba Living coner stone international church Zomba

12/09/2024

Tiyeni tizapemphel limoz this coming Sunday Mulungu azanva zosowa zathu, kuthokoz kwathu kmanso azkhululuk machimo athu mpingowu ukupezeka kuthu pafupi ndi gilesi orphanage

12/09/2024

Yesu ndiye njila yathu tiyeni tintamande

12/06/2022

Hello pipo today is Sunday tiyeni tikapemphele

18/02/2022

Ngati wadzuka ndi mayo ndi chisomo cha Mulungu usangodusa tangolemba amen

15/02/2022

Friends and family don't forget this coming Friday tili ndi
cell

Venue # ku tolls
Time # 3:00pm

Send a message to learn more

03/01/2022

Mulungu ndiyekhayo wankulu amathekesa zinthu zomwe ife anthu zutikanika chikulu nkungokhulupila

Send a message to learn more

13/12/2021

God is good and it's only yemwe angatithandize popeze zinthu like mwayi wa ntchito , kmanso pa ma business athu

11/12/2021

Hello my friend's don't forget about Sunday service
Bwelani nonse izungulila Zomba district
muli olandilidwa ku za Pemphela ku mpingo
wanuwanu ku Zomba kuno
Venue ➖ Grace opharns
Time ➖8 clock Am

Address

Zomba Chikanda
Zomba

Telephone

+265880258147

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zomba Living coner stone international church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share