03/10/2025
mwana wanu amatha kulira usiku, Inu n'kumukalipira makolo m'malo moti mupemphere koma Inu mukungomukalipira kuti mwana akuvuta.
mwana nthawi zonse akamalira pamakhara Pali chifukwa.
dzukani!
pempherani!
usiku uliwonse mwana akalira.
musalore kuti afiti omwe ndi itumikira a Satana akutengereni ana anu ndikuwaphunzitsa ufiti.
Zikomo kwambiri 🙏