Adventist Youth phalombe 2 ZONE 2

Adventist Youth phalombe 2 ZONE 2 This page is for updates on issues concerning zone AY and for posting word of God in these last days.

Ano simalo ocheza nkhani za ndale mpira ai, ano simalo a dating.

10/02/2021

Hello people,
Tiyeni tikumbukire kt ambuye Ali pafupi kubwera, tikamaona zinthu zoopsa ngati covid, njala kuukirana kwa anthu izi zizitikumbusa kt nthaw yatha ndipo posachedwapa mwana wa Mulungu adza kudzaweruza.

30/01/2021

Pamene tikukonzekera in-service training tiyeni tikumbukirenso kuchiikiza chinthuchi mmapemphero

Address

Phalombe

Telephone

+265998314131

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Adventist Youth phalombe 2 ZONE 2 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share