Evangelist Fackson Kondowe. GFC Ministries

Evangelist Fackson Kondowe.  GFC Ministries Malawi

03/01/2026

2026 the year of supernatural growth and increasing 🙏
be blessed

10/12/2025

Mulungu sanayambe alakwitsapo, nthawi Zina nyengo zopweteka zikatifikira timaeona ngati Mulungu alakwitsa. koma Mulungu amalora kuti zitifikire ndi cholinga, chifukwa kuseri kwa nyengo zimenezo kuli chipambano chathu.
Osawopa, osachita mantha, osabwelera mbuyo, Yehova atipambanitsa.

11/10/2025
Heavenly voice. Grace after Grace
15/06/2025

Heavenly voice. Grace after Grace

29/10/2024

Satana sazaleka kulimba nawe. Chifukwa amaziwa chomwe akuwona pa iwe. Koma usachite mantha Mulungu akumenyera nkhondo ndipo upambana.

09/09/2023

Nsanje imapangitsa kuti munthu uchoke pachimene Mulungu anakuyika kupanda kusamala.

Address

Mzuzu

Telephone

+265884028380

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Evangelist Fackson Kondowe. GFC Ministries posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Evangelist Fackson Kondowe. GFC Ministries:

Share