Mzuzu Baptist Church

Mzuzu Baptist Church A religious organization focusing on uplifting lives of all human beings created by God.

20/04/2026

A busa Regie Mhango ochokera ku mpingo wa Mzilaingwe Baptist ati ndi chithu chabwino kuti abusa azigawana upangiri ufuna kutukula mpingowo.

Iwo akufotokoza;

20/04/2026

Mu vidiyo iyi a Busa Burton Kamija Nyirenda akufotokoza za masomphenya a zaka zitatu zikubwerazi.

‎Komiti ya tsopano ya a busa mu mpingo wa Baptist yili mchigawo chakumpoto pofuna kugawana masomphenya a komitiyi a mu z...
20/04/2026

‎Komiti ya tsopano ya a busa mu mpingo wa Baptist yili mchigawo chakumpoto pofuna kugawana masomphenya a komitiyi a mu zaka zitatu zikubwelazi, abusa ochokera mmadera osiyanasiyana mu mpingowo anakhala pamodzi pa likulu la mpingowu la Baptist Church ku Mzuzu.

‎ A Burton Kamija Nyirenda omwe ndi Mtsogoleri wa Bungwe la abusa komanso ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa Baptist convention of Malawi BACOMA akuyendera abusa mzigawo zonse mu Malawi ndicholinga chogawana masomphenya awo pokhala kuti alowapo kumene pampandowu pamodzi ndi alembi awo.

26/03/2026

According to Dr. Gideon Manda, the chairperson of the organizing committee, there was a significant gap in how pastors minister the Word of God to their followers.

Manda, who is also a pastor, explains more in this video.

Mkumano uwu wayima pa Machitidwe 20 v 17 kumatsika mmunsi.
26/03/2026

Mkumano uwu wayima pa Machitidwe 20 v 17 kumatsika mmunsi.

26/03/2026

Msonkhano wa masiku awiri omwe wakonzedwe pofuna kuthandiza atumiki a mpingo yosinasiyana ku Mzuzu powakumbutsa zolinga za utumiki wao uli mkati pomwe M'busa Dr Chris Anderson ochokera ku United States - Florida ndiomwe akuchititsa ziphunzitsozi.

Mu vidio iyi Dr Anderson ali mkati mophunzitsa abusa osiyanasiyana pa mpingo wa Mzuzu Baptist Church.

18/03/2026

Ife tayamba zokonzekera za la Mulungu likubwerali kudzayimbira Yehova.

Ponyani video yanu mu comment box yazokonzekera zanu tionere nao

15/03/2026

Ndikuthokoza makwaya onse amene anaonetsa chidwi pokhalapo pachilinganizo ichi, Happy Gama wapampando wachilinganizo

15/03/2026

The Mzuzu Baptist Youth choir Association successfully hosted its inaugural choir competition over the weekend, an event designed to foster leadership and unity among young congregants.
‎While the association had extended invitations to 35 church choirs across the region, only four managed to participate due to financial constraints related to registration fees.

‎Mzuzu Youth Association chairperson, Happy Gama, emphasized that the primary goal remains collective growth, stating the competition serves as a platform to "learn from each others' mistake."
‎With a total purse of 240,000MK on the line—awarding 100,000MK to the first winner, 80,000MK to the second, and 60,000MK to the third.
‎Pastor Francis Kisebe of the Mzuzu Baptist Church reinforced the developmental vision, noting that such events are crucial for "building church leaders while unifying the youths,"

13/02/2026

Kuyimbira Yehova ndikokoma, nanga Inu?

Address

Mzuzu Baptist Church, PO Box 551
Mzuzu
MWM

Telephone

+265999088769

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mzuzu Baptist Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Mzuzu Baptist Church:

Share