Chibavi Baptist Church

Chibavi Baptist Church Chibavi Baptist Church is a member of Baptist Convention of Malawi (BACOMA). Found in Mzuzu City of the Northern Region of Malawi.

1. MAKHALIDWE A MUNTHUNdime 1-4a. Adzala ndi mkwiyo wa uchimo ndime 1,2,3-4b. Sitidziwa/sitionamo chabwino mwa iye ndim...
08/09/2024

1. MAKHALIDWE A MUNTHU Ndime 1-4

a. Adzala ndi mkwiyo wa uchimo ndime 1,2,3-4

b. Sitidziwa/sitionamo chabwino mwa iye ndime 3

2. MAKHALIDWE A MULUNGU Ndime 5-8

a. Alingalira za anthu
b. Ndi wachisomo ndime 6-7
c. Okoma mtima ndime 8
d. oleza mtima
e. Wodzadza ndi chikondi
f. Okhululukira machimo

MALO: CHIBAVI BAPTIST CHURCHMLALIKI: Pastor M MwalweniUTHENGA: MULUNGU NDI WOSIYANA NDI MUNTHUNDIME: Yona 4:1-4Pa Yona 4...
08/09/2024

MALO: CHIBAVI BAPTIST CHURCH

MLALIKI: Pastor M Mwalweni

UTHENGA: MULUNGU NDI WOSIYANA NDI MUNTHU

NDIME: Yona 4:1-4Pa Yona 4:1-4 pali kusiyana kuwiri muchikhalidwe pakati pa munthu ndi Mulungu komwe tiyenera kuzindikira kuti tikayamikire chipulumutso chathu ndi kukatamanda/kumuyamikira Mulungu

Brother Samuel Nkhoma preaching.....
11/08/2024

Brother Samuel Nkhoma preaching.....

11/08/2024
11/08/2024

Kotero kuti ifeyo tiyeni tikaonetsere Chikondi Cha Mulungu kwa iwo onse asowekera Chikondi Cha Mulungu posatengera chomwe iwo Ali komanso ife tili. Izi ndi zomwe msamariya wa chifundo akutiphunzitsa.

Mulungu akudalitseni nonse.

11/08/2024

(iii) aliyense yemwe asowekera Chikondi Cha Mulungu kudzera mwa ife vs 35-37.

11/08/2024

(ii) yemwe akhala nawo makhalidwe kapena zintchito zochitira chifundo anansi ake. Vs 33-35

11/08/2024

(i) Mnansi wathu ndi munthu yemwe achita chilungamo ndinso akahala muchilungamo kuchoke mtima. Vs 30-33
Machitachita a chipembedzo sindicho chikhristu chenicheni koma kuchita cholungama.

11/08/2024

Sunday Service 11/08/2024
Mlaliki: Brother Samuel Nkhoma
Buku: Luka 10:30-37; 25-29
Mutu: KODI MNANSI WANU NDANI?

With a heavy heart, Chibavi Baptist Church wishes to announce the death of Pastor Rodney Banda of Karonga Baptist Church...
21/07/2023

With a heavy heart, Chibavi Baptist Church wishes to announce the death of Pastor Rodney Banda of Karonga Baptist Church. Prior to the call for the role of Pastor, Banda was a long and dedicated Church elder for Chibavi Baptist Church. On 30th April, 2023 the Church held a farewell function for him as he was leaving Chibavi Baptist to assume his new role at Karonga Baptist Church.

Unfortunately, today the 21st July, 2023 Chibavi Baptist held another farewell for Banda, the farewell that will make members see him no more.

May the Soul of Pastor Rodney Banda rest in everlasting peace

Address

Mzuzu

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 16:00 - 18:00
Thursday 14:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 06:45 - 18:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chibavi Baptist Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share