Prophet David Kubali

Prophet David Kubali Leader and founder of the Oracle Global Christian church and Yadah Investments.

Mwadziwapo ndani apa?Akutanipo?
11/08/2026

Mwadziwapo ndani apa?
Akutanipo?

Eshii, Ambuye  moyo wathuwu ndiwanu
08/08/2026

Eshii, Ambuye moyo wathuwu ndiwanu

Ndinu Mulungu wamakamu, sinthani nyengo za aliyense anene AMEN pano
08/08/2026

Ndinu Mulungu wamakamu, sinthani nyengo za aliyense anene AMEN pano

08/08/2026

Anzathu lunch iyi mwaphika chani?

Lero mamawa wuno chinandikomera kuyendera nyumba ya Michael Kubali Ndagwada apa mpomwe pali manda a malemu bambo anga ad...
07/08/2026

Lero mamawa wuno chinandikomera kuyendera nyumba ya Michael Kubali
Ndagwada apa mpomwe pali manda a malemu bambo anga adasungidwa muchaka cha 1994 ndili ndi masabata awiri akubadwa .

Mu zimu wanu upitilize kuwusa mtendere madala

Ndife agonjetsi!
06/08/2026

Ndife agonjetsi!

Zokoma ndi zakuyaja zidzakutsatani masiku onse amayo wanu chifukwa Mulungu wamakamu ali mbari yanu nthawi zonseee
06/08/2026

Zokoma ndi zakuyaja zidzakutsatani masiku onse amayo wanu chifukwa Mulungu wamakamu ali mbari yanu nthawi zonseee

04/08/2026

Mukolelesye YESU wanganya

Chisomo cha ndalama  chisefukire pa Inu Chaka chino mu dzina la Yesu Christ
04/08/2026

Chisomo cha ndalama chisefukire pa Inu Chaka chino mu dzina la Yesu Christ

Pomwe adani ako akufalitsa nkhani zoti unatha, Mulungu awalitse nyali pa Inu mu dzina la Yesu
04/08/2026

Pomwe adani ako akufalitsa nkhani zoti unatha, Mulungu awalitse nyali pa Inu mu dzina la Yesu

Address

Mzuzu

Telephone

+265887456954

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Prophet David Kubali posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Prophet David Kubali:

Shortcuts

Share