06/01/2026
THE YEAR OF ABUNDANT GRACE
DAY 2/30 OF PRAYER & FASTING
Petition
📌We should pray for the manifestation of Abundant Grace upon the church and the congregation as per this year's theme.
2 Corinthians 9:8
Tipemphere kukwaniritsidwa kwa chisomo chodzala pa mpingo komanso mamembala mogwirizana ndi mutu wathu wa chaka chino.
2 Akorinto 9:8
Tikumana 5pm ku church tonse kuti tikamalizire limodzi. Zikomo