GOD POWER MEDIA

GOD POWER MEDIA BIBLE STUDY
CHOLINGA CHANGA NDI
2 Timoteyo 3:16
othandiza pophunzitsa, podzudzula, pokonza cholakwika ndi polangiza za chilungamo
(3)

27/08/2026

Moyo mulikunipa ine Chiuta wane //
Uli mmawoko yinu ine khuwonga //

BACK TO THE SENDER VERSESBIBLE STUDYMlaliki 10:8 Wokumba mbuna adzagwamo; ndipo woboola mpanda njoka idzamluma.Mwaona mu...
26/08/2026

BACK TO THE SENDER VERSES
BIBLE STUDY

Mlaliki 10:8 Wokumba mbuna adzagwamo; ndipo woboola mpanda njoka idzamluma.

Mwaona mulaliki akuti okumba mbuna adzagweramo yekha

**Which means ose amene amakuchitila zoipa Mulungu adzambwezera so it's like back to the sender

Yesaya 49:26 Ndipo ndidzadyetsa iwo amene atsendereza iwe ndi nyama yao yao; ndi mwazi wao wao; iwo adzaledzera monga ndi vinyo wotsekemera; anthu onse adzadziwa kuti Ine Yehova ndiri Mpulumutsi wako, ndi Mombolo wako, Wamphamvu wa Yakobo.

************************
*Yesaya akunena kuti ose otsendereza iwe ndidzawadyetsa nyama yawo yawo.

Aroma 12:19 Musabwezere coipa, okondedwa, koma patukani pamkwiyo; pakuti kwalembedwa, Kubwezera kuli kwanga, Ine ndidzabwezera, ati Ambuye.

***
Aefeso 6:12
Pakuti sitikulimbana ndi thupi ndi magazi, koma tikulimbana ndi maufumu, maulamuliro, mphamvu za dziko la mdima, ndi mphamvu zoyipa kwambiri zauzimu zamlengalenga.

Amen.
Denzo Mo Sakuwa

Follow

26/08/2026
26/08/2026

Ali mpopano ambuye yesu ��
Let's worship and praise The Lord

MULUNGU AKUMBUKILESO NYUMBA YANU.🪻🍀🪻🪻🌽🪻NDIPO NYUMBA YANU ITSEFUKILE NDI UREMERELO WA MLUNGU 🍀 🪻 🍀 Yesaya 61 Chaka chimen...
25/08/2026

MULUNGU AKUMBUKILESO NYUMBA YANU.🪻🍀🪻

🪻🌽🪻NDIPO NYUMBA YANU ITSEFUKILE NDI UREMERELO WA MLUNGU 🍀 🪻 🍀

Yesaya 6
1 Chaka chimene mfumu Uziya anamwalira, ndinaona Ambuye atakhala pa mpando waufumu, wautali ndi wokwezedwa, ndipo mkanjo wawo unali wautali; kotero kuti unadzaza mʼNyumba ya Yehova.

2 Pamwamba pawo panayimirira Aserafi, aliyense anali ndi mapiko asanu ndi limodzi: awiri anaphimba nkhope zawo, awiri anaphimba mapazi awo, ndipo awiri ankawulukira.

3 Ndipo Aserafiwo amafuwulirana kuti “Woyera, woyera, woyera Yehova Wamphamvuzonse. Dziko lonse lapansi ladzaza ndi ulemerero wake.”

4 Chifukwa cha kufuwulako maziko a zitseko ndi ziwundo anagwedezeka ndipo mʼNyumba ya Yehova munadzaza utsi.
Denzo Mo Sakuwa

NYIMBO KOMASO MA BIBLE ZIKUGAWIDWA MWA ULERE NDI BUNGWE LA THE GIDEON KODI INU ZAKUPEZANI UKO?🏃♥️Deuteronomo 31:19Ndipo ...
24/08/2026

NYIMBO KOMASO MA BIBLE ZIKUGAWIDWA MWA ULERE NDI BUNGWE LA THE GIDEON KODI INU ZAKUPEZANI UKO?🏃♥️

Deuteronomo 31:19
Ndipo tsopano mudzilemberere nyimbo iyi, ndi kuphunzitsa ana a Israele iyi; muiike m'kamwa mwao, kuti nyimbo iyi indichitire mboni yotsutsa ana a Israele.

Deuteronomo 31:21
Ndipo kudzakhala, zitawafikira zoipa ndi zovuta zambiri, nyimbo iyi idzachita mboni pamaso pao; popeza siidzaiwalika m'kamwa mwa mbeu zao; popeza ndidziwa zolingirira zao
azichita lero lino, ndisanawalowetse m'dziko limene ndinalumbira.

NGATI MUKUFUNA KUZIWA ZAMBIRI TUMIZANI MESSAGE KU GOD POWER MEDIA komaso KuDenzo Mo Sakuwa

23/08/2026

Yakobo 4:4
Akazi achigololo inu, kodi simudziwa kuti ubwenzi wa dziko lapansi uli udani ndi Mulungu? .

BWERANI MUZAGULE MA BIBLE PA MTENGO WA K25 000 Yohane 1:1Pachiyambi panali Mawu, ndipo Mawu anali kwa Mulungu, ndipo Maw...
22/08/2026

BWERANI MUZAGULE MA BIBLE PA MTENGO WA K25 000
Yohane 1:1
Pachiyambi panali Mawu, ndipo Mawu anali kwa Mulungu, ndipo Mawu ndiye Mulungu.
Yohane 1:2
Mawuwa anali ndi Mulungu pachiyambi.
Yohane 1:3
Zinthu zonse zinalengedwa ndi Iye; ndipo popanda Iye sikukanakhala kanthu kalikonse kolengedwa.
Yohane 1:4
Mwa Iye munali moyo, ndipo moyowo unali kuwunika kwa anthu.

AMENE MULI KU DOWA MUNKHOZA KUTIPEZA PA MPONELA TRADING CENTER ,
AMENE MULI MU LILONGWE MUNKHOZA KUTIPEZA KU COOPARATE MORE ,MMBALI MWA M1 KUMA ROBOT 🙏

NGATI MUKUFUNA KUZIWA ZAMBIRI messenger to
👉 Denzo Mo Sakuwa

KUGONA NDI CHIZOLOWEZI CHATHU KOMA KUZUKA NDI MOYO ND CHISOMO KOMANSO CHIFUNIRO CHA MULUNGU INGOLEMBA "AMEEN" NGATI UKUK...
21/08/2026

KUGONA NDI CHIZOLOWEZI CHATHU KOMA KUZUKA NDI MOYO ND CHISOMO KOMANSO CHIFUNIRO CHA MULUNGU INGOLEMBA "AMEEN" NGATI UKUKHULUPILIRA KUTI NDI AMBUYE ZONSEZI

👉tikunena pano azathu Ena Ali mmanda ,
👉Ena alithatha nayo imfa😥
👉Ena lero amwalira inuso NDI mboni tsiku la lero mukupita Ku maliro aujeni Aja , izi zikuonesera chikondi cha mulungu pa Ife tazuka nawo Moyo ,tamuthokoze mulungu

MORNING 🛌

21/08/2026

Masalimo 5:3
Mmawa, Yehova mumamva mawu anga; Mmawa ndimayala zopempha zanga pamaso panu ndi kudikira mwachiyembekezo.

Address

Mzimba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when GOD POWER MEDIA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to GOD POWER MEDIA:

Shortcuts

Share