CHIKALA CCAP CHURCH

CHIKALA CCAP CHURCH Preaching about Jesus Christ

Lero   Kumalizitsa ntchito yokhoma malata
08/10/2022

Lero Kumalizitsa ntchito yokhoma malata

30/01/2022

MWASWERA BWANJI ABALE NDI ALONGO KONSE KUMENE MULI NTHAWI INO?

Zosakhala bwino,, mvula yoopsa kugwetsa church chathu,😥😥😥
18/02/2021

Zosakhala bwino,, mvula yoopsa kugwetsa church chathu,😥😥😥

14/10/2020

Zikomo kwambiri abale nd alongo nonse amene munabwera kudzakhala nafe pa mwambo wa paper sunday umene tinali nawo pa 11 october,, tikuthokoza kwambiri makamaka chfukwa cha thandizo lanu,, Ambuye akudalitseni nd kubwezeresa pamene munachotsapo......

07/09/2020

Muli bwanji abale ndi alongo konse kumene muli?? Tikukudziwitsani kuti pa 11 October 2020 tidzakhala nd BIG PAPER sunday...... cholinga cha paper sunday imeneyi tikufuna kupeza ndalama zomalizitsira kukonza church komanso kulipira anthu ogwira ntchito,,, Ambuye akhale nanu pamene mukukonzekera kudzakhala nafe patsikuli,,,,, zikomo

23/05/2020

Mwadzuka bwanji abale ndi alongo?

21/05/2019

Good morning anthu amulungu

Address

Mulanje

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CHIKALA CCAP CHURCH posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to CHIKALA CCAP CHURCH:

Share

Category