Pastor Anold limbikani likaka

Pastor Anold limbikani likaka Sharing the gospel of our lord jesus to all human race

15/07/2023

Muzipemphera kwambiri chifukwa abale ena ndiwo adani akuru amangofuna mutafa, amafuna zanu zizingolephereka, yes tsogolo lanu likhale lokufa ndipo loto lanu lisakwanilisidwe.
Joseph akudedwa ndi abale ake kamba kaloto lomwe adalota. Ndithu mpaka kupanga plan yoti amuphe ati chifukwa cha loto. " Muoneni olota lota uja akubwera tiyeni timuphe" adakambilana izi yosefe akubwera chapakatari!
Some relatives are so wicked that they may kill you!

16/06/2023

Ah oh okay!
Moyo uno uli ndi nyengo; nyengo zolimba, zowawa ndipo zopweteka. Nyengo zimene anthu aziko la pansi ndithu amafutuka, amatuntha inde safuna kukuyandikiza, amathawa! Kuwayimbira phone amadura, ukaimbanso simapezeka amakhala atazimitsa kuopa k*t uwapemoha!
Inde zikafika potero umalakalaka mwina kungozipha chifukwa moyo umaoneka opanda tanthauzo kwa iwe!
Lero ndimati ndikuuze bale k*t usaziphe, usazimangilire, usamwe pision ndipo usachose moyo wako chifukwa cha mavuto! Ziwa k*t yehova sadakusiye ndipo suli wekha, ziwa yehova akukukonzera umboni.
Masalmo27:10 imati wandisuya atate wanga komanso Mai wanga koma ambuye anditola ine"!
Yes zikuwawa komatu pisachedwa ukhala mboni yeni yeni! Mwa iweyo muli potential that's why nyengo zikulimba, yes uli ndi mdalitso ndiye sungaduse muzofewa!

Taonani Joseph onani David, onani jephita ndipo tawaoneni ana a isreal, muoneni yobu ndipo musaiwale za nowa osema chombo uja k*t anthu adamuseka kwambir ndi kumunyoza zedi! Iwe ukunyozedwa ndipo moyo wako ulibe tanthauzo kwa iwo nduthu koma ziwa mmawa lako walisunga yehova ndipo ndilowala. Azabwera kwa iwe nazakugwadira, azapempha tgandizo lako ndipo azafuna ukhale mfumu yawo! "Khala wa mohavu nulimbike mtima! #

10/06/2023

Lero ndiyankheko izi motere:
Kodi kupemphera mpaka kulira kumakhala kuchuluka kwa machimo?
Eti zoona kuvina church mpaka thuk*ta anga alezera?

Aphwanga kulira kuja sikumakhala kuchuluka kwa machimo mwamva?
Kuduka makolasi kuja simowanso mwamva?
Tachokera kosaziwika, takwera mapiri. Tadusa nkhalango zowulira, taoloka misinje yozama moti akadapanda ambuye kukhala mbali yathu sibwezi tili moyo ndipo sibwezi tili level yomwe tili lero.

Mulungu watichilitsa nthenda ife
Mulungu watipasa ana
Mulungu watipasa ntchito ndi business
Mulungu watipasa banja!
Mulungu wakhala thandizo lathu since day yomwe tinabadwa!
Enafe sitinayamwe bere la mayi wathu koma yehova watilera!

Inutu mwina munabadwa banja lochita bwino, simudasowe chakudya, school fees ndi zovala motero moyo want wangodusa mofewa! Kumaliza secondary straight ku college then straight pa ntchito pomwe enafe takuluk*tika k*t tiphunzire ingakhale k*t tipeze ntchito yosesa mu nsika!
Ndiye tikakumbuka komwe tachoka ndithu chisoni chimatigwira ndipo tilibe chomwe tingamupase mulungu posonyeza kuyamika motero timangopereka moyo wathu onse, mphavu zathu, mzimu wathu ndi thupi lathu k*t zilambire iye!
#
Psalms 10:1-3
Psalms 23:1-5

29/04/2023

Poona k*t a isreal akuchuluka komanso akupindura farao analamula anthu ake k*t aziwazunza a isreal komanso analamula anamwino k*t azipha ana amuna omwe azimai a isreal angabeleke poopa k*t angaputilire kuchuluka ndi kuwaposa mphavu!
Komatu mochuluka momwe adawazunzira momwemonso adali kuchurukira kufikira k*t mose anabadwa ndipo anakulira nyumba ya farao yemwe ndi mdani wamkuru wa isreal!

Ndikufuna ndinene kwa inu k*t oipa samakuonerani kukondwa ndipo ayesesa kukugwetsani , kuk*thirani matope ngakhale kukupekerani nkhani za bodza k*t zanu zide basi! Eya ati banja lanu lithe, business ithe, ntchito akuchoseni!
Ndithu nkhondo zina zimangozuka poona chipambano chomwe yehova wakupasani!
Muzonse zomwe mukudusamo musagwe mphwayi muli ndi mulungu amenya nkhondo zanu ndipo mupambana!!!!

26/04/2023

Muchigwa chozala ndi mafupa owuma mulungu anayankhula ndi Ezekiel k*ti "Kodi mafupa awa mkukhalanso ndi moyo? Ndipo Ezekiel adayankha nati " muziwa ndinu ambuye. Ndipo mulungu adati nenera moyo kumafupa awa ndipo mafupa adakhala ndi moyo!
Lazarus atamwalura ndikukhala mmanda kwa three days yesu akufika pa mandawo ndik*tankhula " Lazarus tuluka ndipo ak*tuluka ndikukhala ndi moyo!
Lero lino ndik*tankhula moyo pa ntchito yako,
Moyo pa business
Ndipo banja lako lilandilenso moyo!
Yehova mulungu ndo wazatheka bwanji.amapanga zosatheka kukha zotheka.zomwe wakhala ukuchita koma osapindula nazo ndikulankhula mudzina la ambuye wathu yesu khristu k*ti zitheka tsopano!
Anachezera usiku onse achina Petro osapha nsomba koma yesu atawauza k*ti kankhiani kwakuya nimuponye makoka anakola nsomba zochuluka zedi!
Lero ndikunenera mudzina la yesu k*t muona chipambano mudzina la yesu khristu!
Mmimba youma ilandire mamasulidwe nibale.
Nthenda zosamva mankhwala zilandire machilitso mudzina la yesu khristu!

Ndinu odalitsika ero mudzina la yesu khristu!!!

25/04/2023

Ok madzuro abwino kwa nonse! Ambuye amakukondani kwambiri!
Madzuro uno ndimati ndilimbikiseko anthu amene muk*tonzedwa, kunyozedwa kolapisa kamba ka nyengo zomwe mukudusamo! Ena akuyankhura zok*tembelerani ndipo ena akunyoza ntchito yomwe mumagwura, maganyu omwe mumachitira, business yanu ngakhale zaulimi. Ndimati ndiyankhula nanu motere:
(1) mesiboseti olumala okhala kulodebala odya zotoleza siku lina yehova adamukumbukira ndipo adadya pamodzi ndimfumu nakhala pamaso oa mfumu masiku onse amoyo wake.
2)pamene nows amkasema chombo anthu adanyoza mkumati anowa apenga komatu nowa sadaeamvere ndipo sadakhumudwe adapitiliza kusema chombo poziwa k*t siku lina azapulumukira chombo chimenecho mwa ichi usamade nkhawa ndionyoza chifukwa sakuziwa komwe mulungu akukupitisa komanso sangadyese family yako.
3) loto lomwe yosefe adalota lidausa nsanje pakati pa abale ake. Nthawi zina nkhondo zimazuka kamba kachomwe mulungu waikiza pa iwe kapena chomwe wakukonzera patsogolo mwa ichi imabe nga nga nga pa loto lako ndi maso mphenya ako!

25/04/2023

Let me tell you this " kumwamba kuli mulungu osintha nyengo"! Mulungu opanga njira popanda njira, mulungu otimenyera nkhondo! Mukawelenga Exodus 8 muona zwe mulungu akuchita pa farao yemwe akuzuza ana amulungu!
Mukawelenga Exodus 14 muona yehova wamaku akugawa nyanja k*ti ana ake awoloke pouma! Daniel 3 akupulumutsa achina shadrick, miseck mdi abidenego!
Pa nyengo ili yonse yomwe mukudusamo yehova wamaku ak*tulusani ndipo ziwani k*t sali chete!
Iye amasamala za ife!
Musazimangilire,musachose moyo kamba kanyengo koma maka itanani pa dzina lake!

24/04/2023

Siku lina kunacha batumeyo Ali wakhungu!
Namaan Ali wa khate
Ndipo Lazarus ali manda !
Koma pomwe zuwa la siku limenero limaliwa anthu awa nyengo zawo zidali zitasintha! Batumeyo adalandira kuona kwake, naye namaan khate lidatha pomwe Lazarus anaukisidwa kwa kufa!
Chili chonse chili ndi nyengo komanso nthawi. Yehova ayendere nyengo zako lalero ndipo vuto lako alithese, mudzina la yesu!!?

23/04/2023

Good morning!
I have received more messages inbox that says my help line number :0993683266 is out of reach! Now let me tell you that you can connect with me through that number on WhatsApp only but other numbers on posters are for direct calls, SMS and even WhatsApp!
Ilost the number 0993683266 but someone helped me to keep using it through WhatsApp since many people know only that number!
Have blessed Sunday morning

22/04/2023

Anthu atha kukukanani lero kamba ka nyengo zomwe mukuduso ndipo ena kumakunyozani koma ndati ndikulimbikiseni k*t yehova sanak*tayeni Ali nanu

19/02/2023

Have choosen not to fear in the most fearless land but fighting amaleki lifting the hand of God. Exodus17:16 the Lord will be at war against the Amalekites from generation to generation.”

02/02/2023

Purpose Greater than Ourselves

“And he who does not take up his cross and follow Me [cleave steadfastly to Me, conforming wholly to My example in living and, if need be, in dying also] is not worthy of Me.”Matthew 10:38 (AMPC)

To take up the our cross and follow Jesus has everything to do with living in and for Him, and not ourselves. Just like Him, we are here for a purpose that is greater than ourselves. So we lay everything down, including our pride and popularity, to fulfil the assignment we were created to do. In Philippians 3:10, Paul speaks about this determined purpose: to know the Person of Jesus more; to know the power of His resurrection; and to share in His sufferings. All of which would cause us to be completely transformed into the likeness of Jesus. The sufferings Jesus and Paul are referring to have nothing to do with punishment for sin, nor anything Jesus overcame on the cross. That was a burden only He was worthy to die for. Rather, the suffering we all need to go through is resisting the kingdom of darkness that oppose everything Jesus paid for to see us live in. 1 Peter 5:8-10 speaks of this very truth. We are warned to be extremely vigilant concerning our adversary, the devil, and his intention to destroy every good thing God has done. We are to constantly resist him, stand our ground in faith, and push back the kingdom of darkness in the authority Jesus has given us, in spite of the persecution it will entail. It means laying down our own agendas, popularity, and will to the Lord, and living completely for Him and His cause! This suffering includes constantly dying to our old sinful nature, and embracing the new, renewed life we have in Jesus – a daily battle that requires everything of us. Then we are well able to enforce the devil’s defeat on this earth and release the love and power of God over people’s lives wherever we go.

Address

Lilongwe
Lilongwe

Telephone

+265993683266

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pastor Anold limbikani likaka posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Pastor Anold limbikani likaka:

Share