Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD

Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD Therefore go and make disciples of all nations, baptizing them in the name of the Father and of the Son and of the Holy Spirit (Matthews 28v19)

Msambachikho CCAP is one of churches under the Nkhoma CCAP Synod and is situated in Area 38, Lilongwe, Malawi

23/08/2026

Takulandilan kuchipembedzo cha chiwili cha Chichewa khalani omasuka pamene tikupembedza Limodzi.

23/08/2026

Msambachikho CCAP

The main speaker Rev. K.Kaphaiye Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD
19/08/2026

The main speaker Rev. K.Kaphaiye Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD

18/08/2026

Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD

Gulu la abambo a Msambachikho CCAP kuyimba nyimbo nthawi ya chipembedzo motsogozedwa ndi Rev Kapaiye.

Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD Gulu la Abambo a Msambachikho CCAP Lachita Ulendo Wophunzira ndi Gulu la Abambo a St. Col...
18/08/2026

Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD
Gulu la Abambo a Msambachikho CCAP Lachita Ulendo Wophunzira ndi Gulu la Abambo a St. Columbus CCAP (14-16 August.26)

Kumapeto kwa sabata yapitayi, Gulu la Abambo a Mpingo wa Msambachikho CCAP linachita ulendo wokacheza ndi kuphunzira kuchokera ku Gulu la Abambo a Mpingo wa St. Columbus CCAP, wa Blantyre Synod.

Pa ulendowu, Head of the Church wa Msambachikho CCAP, Rev. Kaphayiye, analinso nawo limodzi ndi gulu la abambowa.

Malinga ndi zomwe Msambachikho CCAP Media yapeza, ulendowu unali wopindulitsa kwambiri, chifukwa abambowa anapeza mwayi wophunzira zambiri zokhudza moyo wauzimu komanso moyo wakuthupi, kuphatikizapo mmene angalimbitsire ntchito ya abambo mu mpingo.

Msambachikho CCAP Media inakwanitsanso kulankhula ndi mmodzi mwa abambowa, yemwe anatsimikizira kuti zomwe aphunzira paulendowu sizidzangowathandiza iwo okha, koma zidzapindulitsanso mpingo wonse wa Msambachikho CCAP. Iye anati abambowa akuyembekezeka kugawana ndi kuphunzitsa mpingo zina mwa zinthu zofunika zomwe aphunzira kuchokera ku St. Columbus CCAP, womwe ndi umodzi mwa mipingo yodziwika bwino mu Blantyre Synod.

Ulendowu ukuonedwa ngati gawo lofunika kwambiri lolimbikitsa mgwirizano, kuphunzirana komanso kukula kwa moyo wauzimu pakati pa mipingo ya CCAP.

Olemba Nkhani ndi Kujambula Zithunzi:
Msambachikho CCAP Media
Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD

Chipembedzo Chachiwili cha Chichewa
16/08/2026

Chipembedzo Chachiwili cha Chichewa

Today Service
09/08/2026

Today Service

Address

Box 30868
Lilongwe
265

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Msambachikho CCAP Nkhoma SYNOD posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share