Chileka CCAP Nkhoma Synod

Chileka CCAP Nkhoma Synod Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chileka CCAP Nkhoma Synod, Religious organisation, Chileka CCAP P. O. Box 26 Namitete, Lilongwe.

25/05/2026
Nehemiah adakhudzika m'tima atawona kuti kumudzi kwawo kuli bwinja (Nehemiah 2: 1_20) nanuso mukhudzike m'tima kuona kut...
25/05/2026

Nehemiah adakhudzika m'tima atawona kuti kumudzi kwawo kuli bwinja (Nehemiah 2: 1_20) nanuso mukhudzike m'tima kuona kuti Ku church chanu cha Chileka CCAP kulibe zida inde zikweza mawu ndipo muchitepo kathu

ku Chileka kuja ndikumudzi qanu inde ku church qanu mudzachitepo kathu

mwachiyamba bwanji chitsitsimutso
22/05/2026

mwachiyamba bwanji chitsitsimutso

Azanutu mawa loweluka pa 23 akupita ku joint meeting inuyo bwanji simufuna kulowa Chigwirizano cha anyamata ndi ana ?? a...
22/05/2026

Azanutu mawa loweluka pa 23 akupita ku joint meeting inuyo bwanji simufuna kulowa Chigwirizano cha anyamata ndi ana ?? ayi pangani chisakho kuti nanu mu zachitika ngati izi muzipezeka

mwala , kalawire , Namitondo, station, & Chipanga zone kupita ndi ku Namitondo

khani nja pethekositi inde kubwela qa mzimu woyela
19/05/2026

khani nja pethekositi inde kubwela qa mzimu woyela

Mawa Ku church mupita & Mukapephela kuti ???
16/05/2026

Mawa Ku church mupita & Mukapephela kuti ???

16/05/2026

Mawa osakhala pa Nsambe CCAP ana aja akukakhazilitsa DvD 📀 tikakumane mekoko 🔥🔥🔥 Mwala nursery under Chileka CCAP ili komweko

Address

Chileka CCAP P. O. Box 26 Namitete
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chileka CCAP Nkhoma Synod posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share